Daily Archives: January 24, 2022

Kuyankha Adhaan

Adhaan ndichizindikiro chachikulu chachisilamu. chifukwa choti adhaana ndichizindikiro chachikulu pachipembedzo chachisilamu tikuyenera kuonetsera ulemu ku adhaana ikamapangidwa poyankha, komanso ikamapangidwa osakhala otangwanika ndizinthu zamdziko lapansi. Ndipo sizofunikira pamene adhaana ikuchitika munthu kukhala otangwanika ndikuyankhula zinthu zamdziko lapansi.[1] 1) Pamene ikupangidwa adhaana, yankhani potsatizira mawu amene muadhini (opanga adhaana) akunena.[2] mwachitsanzo …

Read More »