Daily Archives: February 24, 2022

Kupeza nawo duwa yapaderadera ya Angelo

Sayyiduna Aamir bin Rabeeah (radhiyallahu anhu) akulongosora kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adati: Amene angandifunire zabwino angero amamufunira zabwino munthu ameneyo (amampangira duwa) kwa nthawi yomwe iye angamamfunire zabwino Mtumiki (sallallahu alaih wasallam), kotero chisankho chili ndi iye kuchulukitsa duruud kapena kuchepetsa.

Read More »