Uncategorized

Muharram ndi Ashurah

Ndi dongosolo la Allah Ta’ala kuti anadalitsa zinthu zina kuposa zinzake, mwa anthu onse, aneneri ndi omwe adadalitsika kwambiri popatsidwa ulemelero wa pamwamba kwambiri kuposa anthu ena onse, malo onse osiyanasiyana omwe alipo padziko lapansi pano Allah adaidalitsa haramain (Makkah Mukarramah ndi Madinah Munawwarah) kuphatikizapo Aqsa, ndipo pa miyezi 12 …

Read More »

Kuikonzekera Ramadhan

27. Pangani itikafu (M´bindikiro) masiku khumi otsirizira a mwezi wa Ramadan ngati mungakwanitse kutero.

Olemekezeka Ibn Abbas (radhwiyallahu anhu) akusimba kuti, Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adanena zokhudza kukhala mu itikafu kuti: ‘’Munthu amene akupanga itikafu (akubindikira munzikiti) amakhala kutali ndi machimo ndiponso nthawi yomweyo amalandila mphotho za ntchito zomwe akadatha kuzigwira pamene iye asali mu itikaafu.

 

Read More »

Kuikonzekera Ramadhan

15. Pamene muli m’mwezi wa Ramadhan yesetsani kupanga ntchito zabwino. Hadith ina ikuti, ntchito ina iliyonse yabwino yomwe ungachite mwakufuna kwako (nafil ibaadah) m’mwezi wa Ramadhan (umalipidwa ndi Allah) ngati wachita chinthu cha faradh (chokakamizidwa kuchita) ndipo ngati wachita ntchito ya farad (yokakamizika kuchita) mumwezi wa Ramadan imaonjezeredwa malipiro ake …

Read More »

Kuikonzekera Ramadhan

8. Pamene Ramadhan ikubwera komanso tili mkati kati mwa Ramadhan yesetsani kumanena dua yotsatirayi: اَللّٰهُمَّ سَلِّمْنِيْ لِرَمَضَانَ وَسَلِّمْ رَمَضَانَ لِيْ وَسَلِّمْهُ لِيْ مُتَقَبَّلًا O Allaah nditetezeni ine pondifikitsa m’mwezi wa Ramadhan (ndili wa thanzi komanso nyonga ndicholinga choti ndipindule kwambiri m’mweziwu) komanso usamaleni mwezi wa Ramadhan kwa ine (poupangitsa kuti …

Read More »