{"id":3722,"date":"2025-09-10T11:00:42","date_gmt":"2025-09-10T09:00:42","guid":{"rendered":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=3722"},"modified":"2025-09-10T11:00:42","modified_gmt":"2025-09-10T09:00:42","slug":"sunnats-ndi-aadaab-za-salaam-8","status":"publish","type":"post","link":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=3722","title":{"rendered":"Sunnats Ndi Aadaab Za Salaam 8"},"content":{"rendered":"<p>26. Ndi adab (makhalidwe a usilamu) kuti pamene munthu wina akuyenda, wina wakhala pansi, ndiye kuti oyendayo ayambe kupereka salaamu ndi kupereka moni. Chimodzimodzinso, pamene wina ali m\u2019sitima yapamadzi ndipo wina akuyenda, ndiye kuti okwerayo ayenera kuyamba kupereka salamu ndi kupereka moni. Chimodzimodzinso, achichepere ayenera kupereka moni kwa akuluakulu, ndipo kagulu kakang\u2019ono (ochepa m\u2019chi\u0175erengero) kayenera kupereka moni ku gulu lalikulu (ochuluka).<\/p>\n<p style=\"text-align: left;\"><em>Olemekezeka Abu Hurairah (radhiyallahu anhu) wanena kuti Mtumiki (Sallallahu alaihi wasallam) adati: \u201cAmene wakwera pachombo ayambilire kupereka salam kwa amene akuyenda. Amene akuyenda apereke salaam kwa amene ali chikhalire.<\/em><\/p>\n<p><strong>Zindikirani:<\/strong> Ngakhale chikhalidwe cha Chisilamu ndikuti magulu awa omwe atchulidwa mu Hadith ayambilire kupereke salaam, komabe aliyense ayesetse kuyambilira popereka salaam, monga momwe zinaliri sunna ya Mtumiki (Sallallahu alaihi wasallam) kuyambilira kupereka salaam akakumana ndi munthu.<\/p>\n","protected":false},"excerpt":{"rendered":"<p>26. Ndi adab (makhalidwe a usilamu) kuti pamene munthu wina akuyenda, wina wakhala pansi, ndiye kuti oyendayo ayambe kupereka salaamu ndi kupereka moni. Chimodzimodzinso, pamene wina ali m\u2019sitima yapamadzi ndipo wina akuyenda, ndiye kuti okwerayo ayenera kuyamba kupereka salamu ndi kupereka moni. Chimodzimodzinso, achichepere ayenera kupereka moni kwa akuluakulu, ndipo kagulu kakang\u2019ono (ochepa m\u2019chi\u0175erengero) kayenera &hellip;<\/p>\n","protected":false},"author":3,"featured_media":3614,"comment_status":"closed","ping_status":"open","sticky":false,"template":"","format":"standard","meta":{"footnotes":""},"categories":[12,31],"tags":[],"class_list":["post-3722","post","type-post","status-publish","format-standard","has-post-thumbnail","","category-masunna-ndi-aadaab-miyambo","category-salaam"],"_links":{"self":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/3722","targetHints":{"allow":["GET"]}}],"collection":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts"}],"about":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/types\/post"}],"author":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/users\/3"}],"replies":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcomments&post=3722"}],"version-history":[{"count":1,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/3722\/revisions"}],"predecessor-version":[{"id":3723,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/3722\/revisions\/3723"}],"wp:featuredmedia":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/media\/3614"}],"wp:attachment":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fmedia&parent=3722"}],"wp:term":[{"taxonomy":"category","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcategories&post=3722"},{"taxonomy":"post_tag","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Ftags&post=3722"}],"curies":[{"name":"wp","href":"https:\/\/api.w.org\/{rel}","templated":true}]}}