{"id":4037,"date":"2026-04-22T17:57:52","date_gmt":"2026-04-22T15:57:52","guid":{"rendered":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=4037"},"modified":"2026-04-22T17:57:52","modified_gmt":"2026-04-22T15:57:52","slug":"sunnats-ndi-aadaab-pa-kumwa-1","status":"publish","type":"post","link":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=4037","title":{"rendered":"Sunnats Ndi Aadaab Pa Kumwa 1"},"content":{"rendered":"<p>1)Musanamwe, Nenani dzina la Allah powerenga<\/p>\n<p class=\"\" dir=\"RTL\" style=\"text-align: center; font-family: 'Traditional Arabic'; font-size: 16pt;\">\u0628\u0650\u0633\u0652\u0645\u0650 \u0627\u0644\u0644\u0647<\/p>\n<p style=\"text-align: center;\"><em>M&#8217;dzina la Allah.<\/em><\/p>\n<p>2) Imwani ndi dzanja lamanja.<\/p>\n<p style=\"text-align: center;\"><em>Olemekezeka Ibnu Umar radhwiyallah anhuma akunena kuti Rasulullah adati, &#8220;Aliyense wa inu akamayamba kudya, ayenera kudyera dzanja lake lamanja, ndipo akamamwa, ayenera kumwera dzanja lake lamanja, pakuti Shaitaan amadya ndi dzanja lake lamanzere ndi kumwa ndi dzanja lake lamanzere.<\/em><\/p>\n<p>3) Ndi bwino osamwera m&#8217;botolo kapena chiwiya chomwe sichikuoneka mkati mwake chifukwa chakuti n&#8217;kutheka kuti mukhoza kukhala chinthu changozi mkati mwa botolo kapena chiwiya (ngati zilombo). M&#8217;malo mwake pakuyenera kuthira mkapu zomwe zili m&#8217;botolozo kenako ndikumwa.<\/p>\n<p>4. Ndi bwino kukhala pansi ndikumwa. Komabe, ngati ndi madzi a Zam Zam kapena madzi omwe amatsalira mchitini pambuyo pa wudhu, ndiye kuti ukhoza kumwa chiimire.<\/p>\n<p>5. Mukamamwa, musameze zakumwa zonse zomwe zili mkapu nthawi imodzi, chifukwa izi zingaononge thupi lanu. M&#8217;malo mwake, muyenera kumwa katatu modukizadukiza. Ngati zili mkapuzo ndi zochepa kwambiri moti munthu angathe kumwa kamodzi kapena kawiri, ndizoloredwa kumwa katatu.<\/p>\n<p style=\"text-align: center;\"><em>Olemekezeka Ibnu Abbaas radhwiyallah anhuma akufotokoza kuti Rasulullah swallallahu alaihi wasallam adati: &#8220;Musamwe mwakamodzi ngati ngamira, koma Imwani modukiza ngati kawiri kapena atatu, ndipo tchulani dzina la Allah mukayamba kumwa, ndipo mtamandeni Allah mukamaliza kumwa.&#8221;<\/em><\/p>\n<p>6. Pamene mukumwa, muthokozeni Allah chifukwa cha chakumwa chimene wakupatsani ponena mawu oti &#8220;Alhamdulillah&#8221;.<\/p>\n<p style=\"text-align: center;\"><em>Olemekezeka Anas radhwiyallahu anhu akusinba kuti Hazrat Rasulullah swallallahu alaihi wasallam adati: &#8220;Ndithu Allah Talaa amasangalala ndi kapolo amene amadya cha chakudya chochepa, kapena kumwa madzi ochepa, ndi kumutamanda Allah (kusonyeza kuyamika) pa zimenezo.<\/em><\/p>\n","protected":false},"excerpt":{"rendered":"<p>1)Musanamwe, Nenani dzina la Allah powerenga \u0628\u0650\u0633\u0652\u0645\u0650 \u0627\u0644\u0644\u0647 M&#8217;dzina la Allah. 2) Imwani ndi dzanja lamanja. Olemekezeka Ibnu Umar radhwiyallah anhuma akunena kuti Rasulullah adati, &#8220;Aliyense wa inu akamayamba kudya, ayenera kudyera dzanja lake lamanja, ndipo akamamwa, ayenera kumwera dzanja lake lamanja, pakuti Shaitaan amadya ndi dzanja lake lamanzere ndi kumwa ndi dzanja lake lamanzere. &hellip;<\/p>\n","protected":false},"author":3,"featured_media":4030,"comment_status":"closed","ping_status":"open","sticky":false,"template":"","format":"standard","meta":{"footnotes":""},"categories":[38,12],"tags":[],"class_list":["post-4037","post","type-post","status-publish","format-standard","has-post-thumbnail","","category-kumwa","category-masunna-ndi-aadaab-miyambo"],"_links":{"self":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4037","targetHints":{"allow":["GET"]}}],"collection":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts"}],"about":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/types\/post"}],"author":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/users\/3"}],"replies":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcomments&post=4037"}],"version-history":[{"count":1,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4037\/revisions"}],"predecessor-version":[{"id":4038,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4037\/revisions\/4038"}],"wp:featuredmedia":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/media\/4030"}],"wp:attachment":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fmedia&parent=4037"}],"wp:term":[{"taxonomy":"category","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcategories&post=4037"},{"taxonomy":"post_tag","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Ftags&post=4037"}],"curies":[{"name":"wp","href":"https:\/\/api.w.org\/{rel}","templated":true}]}}