{"id":4302,"date":"2026-11-03T18:56:13","date_gmt":"2026-11-03T16:56:13","guid":{"rendered":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=4302"},"modified":"2026-11-03T18:57:03","modified_gmt":"2026-11-03T16:57:03","slug":"nkhani-ya-muazzin-wina-yemwemwe-adatuluka-chisilamu-chifukwa-chosateteza-maso-ake","status":"publish","type":"post","link":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=4302","title":{"rendered":"Nkhani Ya Muazzin Wina Yemwemwe Adatuluka Chisilamu Chifukwa Chosateteza Maso Ake"},"content":{"rendered":"<p>Zafotokozedwa kuti nthawi ina panali muazzin wina dzina lake Saalih mumzinda wa Baghdad. Ankadziwika ndi kudzipereka kwake ndipo anadalitsidwa ndi kupanga azaan kwa zaka makumi anayi (40)!<\/p>\n<p>Komabe, kuyang&#8217;ana kamodzi kokha koopsa ndiko kunaononga munthuyu ndipo kunapangitsa zaka zake zonse makumi anayi zopanga azaan kukhala zopanda pake. Anagwa momvetsa chisoni ndipo umu ndi mowe zidakhalira:<\/p>\n<p>Tsiku lina Swaalih ankakwera Minaarat kuti achite azaan, maso ake anayang&#8217;ana pa mwana wamkazi wa mnansi wachikhristu yemwe nyumba yake inali pafupi ndi mzikiti. Atangoyang&#8217;ana, anakopeka ndipo anam&#8217;konda.<\/p>\n<p>Anafika kunyumba kwake nagogoda pakhomo. Mtsikanayo anafuwula kuchokera m&#8217;nyumbamo, &#8220;Ndani ali kumeneko?&#8221; anayankha, &#8220;Swaalih, muazzin.&#8221;<\/p>\n<p>Mtsikanayo atatsegula chitseko, analowa m&#8217;nyumbamo namukumbatira. Mtsikana wachikhristu anadabwa ndipo anafuula kuti, &#8220;Anthu inu (ngati Asilamu) ndi amene anthu amawadalira, ndiye bwanji mukuchita chinyengo chonchi?&#8221;<br \/>\nIye anayankha kuti, &#8220;Ndikufunadi kukhala nawe ndikukukwatira, ndipo ngati siuvomereza kukwatira nane ndikupha.&#8221;<\/p>\n<p>Mtsikana uja anayankha mokwiya kuti, &#8220;Ndili okonzeka kukwatirana nawe ngati utasiya chipembedzo chako.&#8221; Nthawi yomweyo, muazzin adatuluka Chisilamu nati, &#8220;Ndikudzipatula ku Chisilamu ndi ku deen yomwe Muhammad swallallahu alaihi wasallam anabweretsa. Komabe, mtsikanayo sanakhutire ndipo anati, &#8220;Wangolankhula mawuwa kuti undithe, ukathana nane udzabwerera ku Dini yako. Kuti nditsimikizire kuti ukufunadi kukhala ndi ine, idya nkhumba.&#8221;<\/p>\n<p>Mosazengereza, Swaalih anaika nkhumba mkamwa mwake ndikudya. Kenako mtsikanayo anamupempha kuti amwe vinyo, ndipo iye anatero ndi mtima onse.<\/p>\n<p>Pomaliza vinyoyo anakwanirana m&#8217;maganizo mwake ndikumuledzeretsa, anayesa kumuyandikira. Komabe, iye analowa m&#8217;chipinda ndipo anatseka chitseko. Kenako anamuitana nati, &#8220;Kwera padenga la nyumba ndikudikira kuti abambo anga abwere. Akafika ndiye kuti apangitsa nikaah yathu.&#8221;<\/p>\n<p>Kenako Swaalih anakwera padenga, koma chifukwa cha kuledzera, anagwa pansi ndikumwalira.<\/p>\n<p>Mtsikanayo anatuluka nabisa thupi lake ndi nsalu. Pambuyo pake, abambo ake atafika ndipo iye anawauza zomwe zinamuchitikira anatenga mtembo usiku n\u2019kuutaya mumsewu.<\/p>\n<p>Pambuyo pake, anthu atamva za tsogolo la muazzin, ndi kusiya kwake Chisilamu, adataya mtembo wake pa dzala.<br \/>\nKuchokera mu nkhaniyi, tikumvetsa mavuto omvetsa chisoni ndi zotsatira zomvetsa chisoni za munthu amene adaitana azaan kwa zaka makumi anayi.<\/p>\n<p>Tikayang&#8217;ana nkhaniyii, tikupeza kuti kulephera kunabwera chifukwa chosateteza maso ake, ndipo mwina anali ndi chizolowezi choipa choyang&#8217;ana akazi.<\/p>\n<p>Zotsatira zake ndi kuti zidamuchititsa kuti amukonde nkaziyu ndipo zidamubwerwtsera mavuto omwe tawamvawa zomwe gawo loipitsitsa kwambiri ndiko kutuluka chisilamu.<\/p>\n","protected":false},"excerpt":{"rendered":"<p>Zafotokozedwa kuti nthawi ina panali muazzin wina dzina lake Saalih mumzinda wa Baghdad. Ankadziwika ndi kudzipereka kwake ndipo anadalitsidwa ndi kupanga azaan kwa zaka makumi anayi (40)! Komabe, kuyang&#8217;ana kamodzi kokha koopsa ndiko kunaononga munthuyu ndipo kunapangitsa zaka zake zonse makumi anayi zopanga azaan kukhala zopanda pake. Anagwa momvetsa chisoni ndipo umu ndi mowe zidakhalira: &hellip;<\/p>\n","protected":false},"author":3,"featured_media":3556,"comment_status":"closed","ping_status":"open","sticky":false,"template":"","format":"standard","meta":{"footnotes":""},"categories":[24],"tags":[],"class_list":["post-4302","post","type-post","status-publish","format-standard","has-post-thumbnail","","category-minda-ya-chikondi"],"_links":{"self":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4302","targetHints":{"allow":["GET"]}}],"collection":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts"}],"about":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/types\/post"}],"author":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/users\/3"}],"replies":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcomments&post=4302"}],"version-history":[{"count":1,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4302\/revisions"}],"predecessor-version":[{"id":4303,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4302\/revisions\/4303"}],"wp:featuredmedia":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/media\/3556"}],"wp:attachment":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fmedia&parent=4302"}],"wp:term":[{"taxonomy":"category","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcategories&post=4302"},{"taxonomy":"post_tag","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Ftags&post=4302"}],"curies":[{"name":"wp","href":"https:\/\/api.w.org\/{rel}","templated":true}]}}