{"id":4318,"date":"2026-11-16T12:40:13","date_gmt":"2026-11-16T10:40:13","guid":{"rendered":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=4318"},"modified":"2026-11-16T12:41:13","modified_gmt":"2026-11-16T10:41:13","slug":"chifukwa-chimene-allah-adamudalitsira-abu-hurairah-radhiyallahu-anhu-ndi-mpamvu-yokumbukira-mwachangu","status":"publish","type":"post","link":"https:\/\/ny.alislaam.com\/?p=4318","title":{"rendered":"Chifukwa Chimene Allah Adamudalitsira Abu Hurairah (radhiyallahu \u2018anhu) Ndi Mpamvu Yokumbukira Mwachangu"},"content":{"rendered":"<p>Nthawi ina, Abu Hurairah (radhwiyallahu \u2018anhu) adawayankhula anthu nati: \u200e<\/p>\n<p>Anthu inu mukunena kuti, \u201cBwanji Abu Hurairah akufotokoza Mahaadith ambiri kuchokera kwa Rasulullah (swallallahu \u2018alaihi wasallam), pomwe ma Swahaabah ena ngati ma Muhaajireen ndi Ansaaar sakunena mahaadith ochuluka choncho kuchokera kwa Rasulullah (Swallallahu \u200e\u200e\u2018alaihi wasallam)?\u201d \u200e<\/p>\n<p>Chifukwa chake n\u2019chakuti nthawi ya Rasulullah (Swallallahu \u2018alaihi wasallam), abale anga ma Muhaajireen ankatanganidwa ndi kuchita malonda m\u2019misika, pomwe ine ndinkakhala ndi Rasulullah (Swallallahu \u2018alaihi wasallam), ndikukhutira ndi chilichonse chomwe chingaloowe m\u2019mimba mwanga. Ndinkakhalapo nthawi imene iwo kunalibe, ndipo tsopano ndikukumbukira Mahadith a Rasullalullah (Sallallahu \u200e\u2018alaihi wasallam) omwe iwo adawaiwala.<\/p>\n<p>Chimodzimodzinso, abale anga ma Ansaari ankatanganidwa ndi kusamalira minda yawo ya zipatso, pomwe ine ndinali munthu osauka omwe ndidali mgulu la ma Swahaaba osauka otchedwa Ashaabus Suffah (kutanthauza kukhala mu \u200emusjid ya Rasulullah [Swallallahu \u2018alaihi wasallam]). Tsopano ndikukumbukira mahadith a Rasullaullah (Swallallahu \u2018alaihi wasallam) pomwe iwo adaiwala.<\/p>\n<p>Abu Hurairah (radhwiyallahu \u2018anhu) pambuyo pake adatchula chifukwa chomwe Allah Ta\u2019ala adamudalitsira ndi nzeru zodabwitsa komanso chodabwitsa chomwe maSwahaaba ena sanapatsidwe. Iye akunena kuti:\u200e<\/p>\n<p>Nthawi ina, Rasulullah (Sallallahu \u2018alaihi wasallam) akufotokoza za Hadith, iye anauza omwe analipo pamalopo kuti, \u201cAliyense pakati panu amene ayale nsalu yake pansi pamaso panga, mpaka nditamaliza zomwe ndikunena, ndipo pambuyo pake atenga nsalu yake ndikufunda pa thupi lake, adzakumbukira zonse zomwe ndinganene (monga, adzakumbukira mahadith onse omwe angamve kwa ine ndipo sadzaziiwala).\u201d<\/p>\n<p>Abu Hurairah (radhwiyallahu \u2018anhu) akunena kuti, \u201cNditamva izi kuchokera kwa Rasulullah (Swallallahu \u2018alaihi wasallam), nthawi yomweyo ndinatambasula nsalu yanga ndikuiyala pansi pamaso pa Rasulullah (Swallallahu \u2018alaihi wasallam), ndipo Rasulullah (Swallallahu \u2018alaihi wasallam) atamaliza kufotokoza Hadith yake, nthawi yomweyo ndinatenga msalu yanga ndikuikulunga pa thupi langa ndi pachifuwa panga.\u201d \u200e<\/p>\n<p>Kenako anati, \u201cKuyambira nthawi imeneyo, sindinaiwale chilichonse chimene ndinamva kuchokera kwa Rasulullah (swallallahu \u2018alaihi wasallam).\u201d (Saheeh Bukhaari #2047, Saheeh Muslim \u200e#2493)\u200e<\/p>\n","protected":false},"excerpt":{"rendered":"<p>Nthawi ina, Abu Hurairah (radhwiyallahu \u2018anhu) adawayankhula anthu nati: \u200e Anthu inu mukunena kuti, \u201cBwanji Abu Hurairah akufotokoza Mahaadith ambiri kuchokera kwa Rasulullah (swallallahu \u2018alaihi wasallam), pomwe ma Swahaabah ena ngati ma Muhaajireen ndi Ansaaar sakunena mahaadith ochuluka choncho kuchokera kwa Rasulullah (Swallallahu \u200e\u200e\u2018alaihi wasallam)?\u201d \u200e Chifukwa chake n\u2019chakuti nthawi ya Rasulullah (Swallallahu \u2018alaihi wasallam), &hellip;<\/p>\n","protected":false},"author":3,"featured_media":0,"comment_status":"closed","ping_status":"open","sticky":false,"template":"","format":"standard","meta":{"footnotes":""},"categories":[22],"tags":[],"class_list":["post-4318","post","type-post","status-publish","format-standard","","category-sahaabah"],"_links":{"self":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4318","targetHints":{"allow":["GET"]}}],"collection":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts"}],"about":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/types\/post"}],"author":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/users\/3"}],"replies":[{"embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcomments&post=4318"}],"version-history":[{"count":1,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4318\/revisions"}],"predecessor-version":[{"id":4319,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=\/wp\/v2\/posts\/4318\/revisions\/4319"}],"wp:attachment":[{"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fmedia&parent=4318"}],"wp:term":[{"taxonomy":"category","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Fcategories&post=4318"},{"taxonomy":"post_tag","embeddable":true,"href":"https:\/\/ny.alislaam.com\/index.php?rest_route=%2Fwp%2Fv2%2Ftags&post=4318"}],"curies":[{"name":"wp","href":"https:\/\/api.w.org\/{rel}","templated":true}]}}