Daily Archives: November 2, 2026

Ulemu wa Abdullah bin Abbaas (radhiyallahu ‘anhuma) kwa Atsogoleri Akuluakulu

Nthawi ina, Olemekezeka Zaid bin Thaabit (radhwiyallahu ‘anhu) anayamba kukwera ngamila yake. ‎Abdullah bin Abbaas (radhiyallahu ‘anhuma) atamuona akukwera, adathamanga mwachangu, adagwira zingwe za nyamayo ndikumuthandizira kukwera. ‎ Pofuna kupereka ulemu Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma), Zaid (radhiyallahu ‎‎‘anhu) adamulankhula nati, “Ee msuweni wa Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam)! Musachite izi …

Read More »