Tafseer

Tafseer Ya Surah Naba

عَمَّ يَتَسَاءَلُونَ ‎﴿١﴾‏ عَنِ النَّبَإِ الْعَظِيمِ ‎﴿٢﴾‏ الَّذِي هُمْ فِيهِ مُخْتَلِفُونَ ‎﴿٣﴾‏ كَلَّا سَيَعْلَمُونَ ‎﴿٤﴾‏ ثُمَّ كَلَّا سَيَعْلَمُونَ ‎﴿٥﴾‏ أَلَمْ نَجْعَلِ الْأَرْضَ مِهَادًا ‎﴿٦﴾‏ وَالْجِبَالَ أَوْتَادًا ‎﴿٧﴾‏ وَخَلَقْنَاكُمْ أَزْوَاجًا ‎﴿٨﴾‏ وَجَعَلْنَا نَوْمَكُمْ سُبَاتًا ‎﴿٩﴾‏ وَجَعَلْنَا اللَّيْلَ لِبَاسًا ‎﴿١٠﴾‏ وَجَعَلْنَا النَّهَارَ مَعَاشًا ‎﴿١١﴾‏ وَبَنَيْنَا فَوْقَكُمْ سَبْعًا شِدَادًا ‎﴿١٢﴾‏ وَجَعَلْنَا سِرَاجًا وَهَّاجًا ‎﴿١٣﴾‏ وَأَنزَلْنَا مِنَ الْمُعْصِرَاتِ مَاءً ثَجَّاجًا ‎﴿١٤﴾‏ لِّنُخْرِجَ بِهِ حَبًّا وَنَبَاتًا ‎﴿١٥﴾‏ وَجَنَّاتٍ أَلْفَافًا ‎﴿١٦﴾‏ إِنَّ يَوْمَ الْفَصْلِ كَانَ مِيقَاتًا ‎﴿١٧﴾‏ يَوْمَ يُنفَخُ فِي الصُّورِ فَتَأْتُونَ أَفْوَاجًا ‎﴿١٨﴾‏ وَفُتِحَتِ السَّمَاءُ فَكَانَتْ أَبْوَابًا ‎﴿١٩﴾‏ وَسُيِّرَتِ الْجِبَالُ فَكَانَتْ سَرَابًا ‎﴿٢٠﴾‏ إِنَّ جَهَنَّمَ …

Read More »

Tafseer Ya Surah Faatihah

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ ‎﴿١﴾‏ الْحَمْدُ لِلَّهِ رَبِّ الْعَالَمِينَ ‎﴿٢﴾‏ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ ‎﴿٣﴾‏ مَالِكِ يَوْمِ الدِّينِ ‎﴿٤﴾‏ إِيَّاكَ نَعْبُدُ وَإِيَّاكَ نَسْتَعِينُ ‎﴿٥﴾‏ اهْدِنَا الصِّرَاطَ الْمُسْتَقِيمَ ‎﴿٦﴾‏ صِرَاطَ الَّذِينَ أَنْعَمْتَ عَلَيْهِمْ غَيْرِ الْمَغْضُوبِ عَلَيْهِمْ وَلَا الضَّالِّينَ ‎﴿٧﴾‏ Kuyamikidwa konse ndi kwa Allah, Mbuye wa zolengedwa zonse. Wachifundo Chambiri, Wachisoni. Mbuye wa tsiku lachiweruzo. Inu nokha timakupembedzanindipo kwa Inu nokha ndi kumene timakupemphani chithandizo. Tiwonetseni …

Read More »

Tafseer Ya Surah Falaq Ndi Surah Naas

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ قُلْ أَعُوذُ بِرَبِّ الْفَلَقِ ‎﴿١﴾‏ مِن شَرِّ مَا خَلَقَ ‎﴿٢﴾‏ وَمِن شَرِّ غَاسِقٍ إِذَا وَقَبَ ‎﴿٣﴾‏ وَمِن شَرِّ النَّفَّاثَاتِ فِي الْعُقَدِ ‎﴿٤﴾‏ وَمِن شَرِّ حَاسِدٍ إِذَا حَسَدَ ‎﴿٥﴾‏ Nena (iwe Muhammad (Swallallaahu ‘alayhi wasallam): “Ndikudzitchinjiriza mwa Mbuye wa m’bandakucha, ku zoipa zonse zomwe Adazilenga, ndi ku zoipa za mumdima (wa usiku) pamene mdima wake ukufalikira; …

Read More »

Tafseer ya Surah Ikhlaas

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ قُلْ هُوَ اللَّهُ أَحَدٌ ‎﴿١﴾‏ اللَّهُ الصَّمَدُ ‎﴿٢﴾‏ لَمْ يَلِدْ وَلَمْ يُولَدْ ‎﴿٣﴾‏ وَلَمْ يَكُن لَّهُ كُفُوًا أَحَدٌ ‎﴿٤﴾‏ Sura iyi ikufotokoza za chikhulupiriro cha Tawhiyd (umodzi wa Allah Ta’ala mu kakharidwe kake ndi mbiri zake), zomwe ndi gawo limodzi lofunikira kwambiri m’zikhulupiliro zazikulu za Chisilamu. Chikhulupiriro cha Tawheed chinali chinthu chachilendo kwa …

Read More »

Tafseer Ya Surah Lahab

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ تَبَّتْ يَدَا أَبِي لَهَبٍ وَتَبَّ ‎﴿١﴾‏ مَا أَغْنَىٰ عَنْهُ مَالُهُ وَمَا كَسَبَ ‎﴿٢﴾‏ سَيَصْلَىٰ نَارًا ذَاتَ لَهَبٍ ‎﴿٣﴾‏ وَامْرَأَتُهُ حَمَّالَةَ الْحَطَبِ ‎﴿٤﴾‏ فِي جِيدِهَا حَبْلٌ مِّن مَّسَدٍ ‎﴿٥﴾ Manja awiri a Abu Lahab awonongeke, ndipo awonongekeretu! chuma chake sichidampindulire ngakhalenso zomwe adapeza. Posachedwapa adzalowa m’moto wodzadza ndi malawi oyaka, komanso mkazi wake, woipa wonyamula nkhuni …

Read More »

Tafseer Ya Surah Nasr

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ إِذَا جَاءَ نَصْرُ اللَّهِ وَالْفَتْحُ ‎﴿١﴾‏ وَرَأَيْتَ النَّاسَ يَدْخُلُونَ فِي دِينِ اللَّهِ أَفْوَاجًا ‎﴿٢﴾‏ فَسَبِّحْ بِحَمْدِ رَبِّكَ وَاسْتَغْفِرْهُ ۚ إِنَّهُ كَانَ تَوَّابًا ‎﴿٣﴾‏ (Oh Muhammad (Swallallaahu ‘alayhi wasallam)) Kukadzafika chithandizo cha Allah Ta’ala ndi kupambana (kugonjetsa Makka Mukarramah) ndipo ukadzawaona anthu akulowa mu Dina ya Allah ali ambiri, choncho lemekeza ndi kutamanda Mbuye …

Read More »

Tafseer Ya Surah Kaafiroon

بِسْمِ اللَّهِ الرَّحْمَٰنِ الرَّحِيمِ قُلْ يَا أَيُّهَا الْكَافِرُونَ ‎﴿١﴾‏ لَا أَعْبُدُ مَا تَعْبُدُونَ ‎﴿٢﴾‏ وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ ‎﴿٣﴾‏ وَلَا أَنَا عَابِدٌ مَّا عَبَدتُّمْ ‎﴿٤﴾‏ وَلَا أَنتُمْ عَابِدُونَ مَا أَعْبُدُ ‎﴿٥﴾‏ لَكُمْ دِينُكُمْ وَلِيَ دِينِ ‎﴿٦﴾‏ Nena: “E, inu anthu osakhulupirira! Ine sindingapembedze (mafano) amene mukuwapembedza, ndiponso simum’pembedza Amene ine ndikum’pembedza (Allah Ta’ala). Ndipo inu simunhampembedze (Allah) Amene ine ndikumupembedza …

Read More »

Tafseer of Surah Kauthar

Ndithu, Ife takupatsa (ndi kukudalitsa) zabwino zambiri Choncho pemphera Swala kwa Mbuye wako, ndipo pereka nsembe. Ndithu, amene akudana nawe adzadulidwa.

M’surayi Allah Ta’ala akulankhula ndi Mtumiki (Swallallaahu ‘alayhi wasallam) kuti: “Ndithu, Ife takupatsa (ndipo takudalitsa ndi) zabwino zambiri.

Zabwino zochuluka zomwe Hazrat Rasulullah (Swallallaahu 'alayhi wasallam) adadalitsidwa nazo padziko lapansi zikuoneka kudzera mu dzina lake la Mubaarak ndi kukwezedwa ulemu, chipembedzo chake chikupitilira kutukuka ndikukula mphamvu ndi mphamvu, ndi kuchuluka kwa anthu olowa m'chipembedzo cha Allah. Chisilamu chikuchuluka tsiku ndi tsiku.

Read More »

Tafseer Ya Surah Ma’un

Kodi mwamuona amene akukana (za tsiku la) Chiweruzo? iye ndi Yemwe akukankha (ndi kutsekereza) wa masiye, ndipo salimbikitsa Kudyetsa osauka. Mavuto akulu ali kwa amene akuswali, amene akunyalanyaza Swalah yawo. Iwo amene (amachita zabwino) podzionetsera, ndipo amakana kupereka (kapena kubwereketsa) ziwiya zawo ngakhale zinthu zazing’ono (zomwe anthu akuzifuna).

Read More »

Tafseer Ya Surah Quraish

لِإِيلفِ قُرَيْشٍ ‎﴿١﴾‏ اِلٰفِهِمْ رِحْلَةَ الشِّتَآءِ وَالصَّيْفِ ‎﴿٢﴾‏ فَلْيَعْبُدُوا۟ رَبَّ هٰذَا الْبَيْتِ ‎﴿٣﴾‏ الَّذِىٓ أَطْعَمَهُم مِّن جُوْعٍ وَاٰمَنَهُمْ مِّنْ خَوْفِۭ ‎﴿٤﴾‏ Chifukwa cha chitetezo cha ma Quraishi, chitetezo chimene amasangalala nacho m’maulendo awo m’miyezi yachisanu ndi m’nyengo yachilimwe. Kotero akuyenera kupembedza Mbuye wa nyumba yopatulika (Ka’aba), yemwe adawapatsa chakudya chothetsa njala yawo ndi chitetezo ku …

Read More »