Ma Sunnah Ena Onse ndi Aadaab Okhudzana ndi Kudya 1. Musachidandaule kapena kuchipezera vuto chakudya. Olemekezeka Abu Hurairah radhwiyallahu anhu akunena kuti Rasulullah swallallah alaihi wasallam sanachipezereko vuto chakudya. Ngati akufuna kudya ankadya, ndipo ngati sanachifune ankachisiya (popanda kuchipezera vuto). 2. Musadye chakudya chotentha kwambiri. Olemekezeka Asmaa bint Abi Bakr …
Read More »Yearly Archives: 2026
Akazi Kuphunzira Maphunziro 3
Olemekezeka Abdullah bin Mas’uud (radhwiyallahu ‘anhu) apha Abu Jahl
Nkhondo ya Badr itafika kumapeto ndipo Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) ndi maswahaabah atapambana, Rasulullah (sallallahu ‘alayhi wasallam) adauza ma swahaabah kuti, “Ndani atapite kukaona momwe Abu Jahl alili?” Abdullah bin Mas’uud (radhwiyallahu ‘anhu) adapita kukamfunafuna ndipo adapeza kuti ana awiri a ‘Afraa (radhwiyallahu ‘anha) adali atamuvulaza, ndipo anali mu ululu …
Read More »Momwe Adabadwira Nabi Isa (‘alaihis salaam)
Dongosolo la Allah Ta‘ala, kukamba momwe amalengedwera anthu, ndilakuti anthu awiri akakumana munthu amapangidwa. Chinthu choyamba ndi kudzera mwa makolo omwe mbewu ya mwamuna imabzalidwa m’mimba mwa mayi. Chinthu chachiwiri ndi mzimu omwe umalowa m’mimba mwa mwana yemwe sanabadweyo akakwanitsa miyezi inayi. Munthu aliyense amene anabwera padziko lapansi adatsatira njira …
Read More »Akazi Kuphunzira Maphunziro 2
Abdullah bin Mas’uud (radhwiyallahu ‘anhu)
Olemekezeka Abdullah bin Mas’uud (radhwiyallahu ‘anhu) anali mnyamata wamng’ono, akuweta mbuzi za Uqbah bin Abi Mu’ait m’chigawo cha Makkah Mukarramah. Tsiku lina ali kuweta mbuzi, Rasulullah (sallallahu ‘alaihi wasallam) ndi Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) adadutsa pamene ankathawa ma mushrikiin. Popeza chinali chizolowezi cha Aarabu kupereka mkaka kwa odutsa mnjira, Rasulullah …
Read More »Masunnah Ndi Miyambo Ya Pakudya 2
Ma Sunnah ndi Miyambo Musanadye 5. Sambani m’manja musanayambe kudya. Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu anhuma) akusimba kuti Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) adati: Kusamba m’manja usanayambe kudya komanso ukamaliza kumachotsa umphawi, ndipo ndi zochokera mu sunnah ya Ambiya onse (alaihimus salaam). 6. Ndibwino kuti kuvula nsapato usanayambe kudya. Olemekezeka Anas …
Read More »Kufunira Ena Zabwino
Kuchokera mu dongosolo lonse la makhalidwe abwino la Chisilamu, makhalidwe onse omwe Chisilamu chimalimbikitsa ndi odzadza ndi zokopa ndipo amawalitsa kukongola. Kaya ndi kulemekeza okalamba, kapena kuchitira chifundo achinyamata, kapena kukwaniritsa ufulu wa makolo ndi abale anu, zonse zimasonyeza ulemerero wapadera wa Chisilamu. Komabe, moyo wa makhalidwe onse apamwambawa uli …
Read More »Akazi Kuphunzira Maphunziro
Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) Kuyamikira Kuwerenga Quran kwa Abdullah bin Mas’uud (Radhwiyallahu ‘anhu)
Umar (radhwiyallahu ‘anhu) adafotokoza nkhani iyi: Rasulullah (swallallahu ‘alayhi wasallam) ankakonda kulankhula ndi Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) akamaliza kuswali Esha ndikukambirana naye zokhuza Asilamu. Usiku wina, atamilza swalah ya Esha, Rasulullah (sallallahu ‘alayhi wasallam) adayamba kuyankhula ndi Abu Bakr (radhwiyallahu ‘anhu) (zokhudza Asilamu) ndipo inenso ndidali nawo pomwepo. Pambuyo pokambirana, …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu