Daily Archives: February 11, 2026

Kukhala Ndi Mtima Okhululukira Ena

Olemekezeka Waa’il bin Hujr (Radhwiya-Allahu anhu) adali Swahaaba otchuka wa Rasulullah (swallallah alaihi wasallam) yemwe ankachokera dela la Yemen ndipo adali ochokera ku banja lachifumu. Zanenedwa kuti atanyamuka ku Yemen kubwera ku Madinah Munawwarah kudzalowa Chisilamu, asadafike Rasulullah Allah adawadziwitsa ma Swahaabah kuti watsala pang’ono kufika. Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) …

Read More »