Monthly Archives: September 2026

Zotsatira Za Kuipa Kwa Vinyo. Mankhwala Ozunguza Ubongo Ndi Zoledzeretsa

Tikayerekeza dini ya Chisilamu ndi zipembedzo zakale, timapeza kuti Chisilamu sichinangolongosora machimo ndi ntchito zoipa kuti ndi haraam, komanso chinafotokoza njira zomwe zimatsogolera ku uchimo ndi zoipa ngati haraam. Izi zidachitika kuti zimuteteze munthu kuti asagwere mu uchimo. Taganizirani chitsanzo cha mowa chomwe chinali choloredwa m’zipembedzo zakale, koma chanenedwa kuti …

Read More »

Uphungu wa Abdullah bin Abbaas (radhiyallahu ‘anhuma)

Wahab bin Munabbih (rahimahullah) akunena kuti: Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (radhiyallahu ‘anhuma) atasanduka wakhungu (ku ukalamba wake), ndidamutsogolera ku Haram Sharif ku Makkah Mukarramah, komwe anamva gulu la anthu likukangana pakati pawo. Anandipempha kuti ndimulondolere kwa iwo. Atafika kwa iwo, anawalonjera ndi mawu onena kuti “Assalaamu Alaikum”. Anamupempha kuti akhale …

Read More »