Wahab bin Munabbih (rahimahullah) akunena kuti: Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (radhiyallahu ‘anhuma) atasanduka wakhungu (ku ukalamba wake), ndidamutsogolera ku Haram Sharif ku Makkah Mukarramah, komwe anamva gulu la anthu likukangana pakati pawo. Anandipempha kuti ndimulondolere kwa iwo. Atafika kwa iwo, anawalonjera ndi mawu onena kuti “Assalaamu Alaikum”. Anamupempha kuti akhale …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu