Zafotokozedwa kuti nthawi ina panali muazzin wina dzina lake Saalih mumzinda wa Baghdad. Ankadziwika ndi kudzipereka kwake ndipo anadalitsidwa ndi kupanga azaan kwa zaka makumi anayi (40)! Komabe, kuyang’ana kamodzi kokha koopsa ndiko kunaononga munthuyu ndipo kunapangitsa zaka zake zonse makumi anayi zopanga azaan kukhala zopanda pake. Anagwa momvetsa chisoni …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu