Kapempheredwe ka Azimayi

Kapempheredwe ka Azimayi

Mazhab anayi Kuyambira nthawi ya Sayyiduna Rasulullah, ma Swahaabah, Taabi’een ndi zaka mazana zotsatira, akazi ankalamulidwa kuswali m’njira yosiyana ndi Swalaah ya amuna m’magawo ena za swalah. Madhabu onse anayi (omwe ndi Hanafi, Maliki, Shafi’i ndi Hambali) onse amagwirizana pa mfundo yakuti Swalaah ya akazi imasiyana ndi Swalaah ya amuna …

Read More »

Kapempheredwe ka Azimayi

Chilichonse cha chipembedzo cha Chisilamu chokhudzana ndi akazi chimakhanzikika pa kukhala odzichepetsa komanso wamanyazi. Pachifukwa ichi ndi pamene Chisilamu chikulamula amayi kuti azikhala m’nyumba zawo, kukhala obisika kwa amuna achilendo, komanso kuti asachoke m’nyumba zawo popanda chifukwa chenicheni pa Sharia. M’mene mkazi walamulidwira kuswali Swalah yake – kuyambira pa chovala …

Read More »