1. Mulimbikire kuchita ibaadah m’masiku khumi oyambirira a Zul Hijjah. Malipiro aakulu atchulidwa pa ibaadah yomwe ingachitike m’masiku khumi amenewa. Olemekezeka Abdullah bin Abbaas radhwiyallahu anhu wanena kuti Nabiy swallallahu alaihi wasallam adati: “Palibe cholungama chomwe chingachitike tsiku lililonse la chaka chomwe chili chabwino kwambiri kuposa masiku khumi a mwezi …
Read More »Zul Hijjah
Mwezi wa Zul Hijjah uli mgulu la miyezi inayi yopatulika ya kalendala ya Chisilamu. Miyezi inayi yopatulika imeneyi ndi Zul Qa’dah, Zul Hijjah, Muharram ndi Rajab. Malipiro a ntchito zabwino zochitidwa m’miyezi imeneyi amachulukitsidwa, ndipo machimo amene achitidwa m’miyezi imeneyi nawonso amatengedwa kuti ndi oipitsitsa kwambiri. Allah Ta’ala akuti: إِنَّ …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu