Ma Sunnah Ena Onse ndi Aadaab Okhudzana ndi Kudya 1. Musachidandaule kapena kuchipezera vuto chakudya. Olemekezeka Abu Hurairah radhwiyallahu anhu akunena kuti Rasulullah swallallah alaihi wasallam sanachipezereko vuto chakudya. Ngati akufuna kudya ankadya, ndipo ngati sanachifune ankachisiya (popanda kuchipezera vuto). 2. Musadye chakudya chotentha kwambiri. Olemekezeka Asmaa bint Abi Bakr …
Read More »Masunnah Ndi Miyambo Ya Pakudya 2
Ma Sunnah ndi Miyambo Musanadye 5. Sambani m’manja musanayambe kudya. Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu anhuma) akusimba kuti Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) adati: Kusamba m’manja usanayambe kudya komanso ukamaliza kumachotsa umphawi, ndipo ndi zochokera mu sunnah ya Ambiya onse (alaihimus salaam). 6. Ndibwino kuti kuvula nsapato usanayambe kudya. Olemekezeka Anas …
Read More »Kudya
Chisilamu ndi Dini ya padziko lonse. Ndi ya nthawi zonse, malo onse ndi anthu onse. Ndi yangwiro komanso yokwanira, kotero kuti yamuonetsa munthu njira yokwaniritsira malamulo a Allah ndi ufulu wa akapolo ake. Munthu asadafike m’dziko kufikira kumwalira, Chisilamu chakhazikitsa malamulo ndi ziletso zomwe zingamuchititse kuti akhale osangalala. Kupatura kupemphera …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu