1 Mizikiti imatengedwa kuti ndimalo okondedwa kwambiri pamaso pa Allah. عن أبي هريرة رضي الله عنه أن رسول الله صلى الله عليه وسلم قال أحب البلاد إلى الله مساجدها وأبغض البلاد إلى الله أسواقها (صحيح مسلم، الرقم: 671) Sayyiduna Abu Hurairah (radhiyallahu anhu) akufotokoza kuti Mtumiki (Sallallahu alaih wasallam) adati: …
Read More »Yearly Archives: 2022
Zofunika za Dunya ndi Aakhirah Zikwaniritsidwa chifukwa chowerenga Durood tsiku la Jumuah
Hazrat Anas bun Maalik (radhiyallahu ‘anhu) akusimba kuti Hazrat Mtumiki (sallallahu ‘alaihi wasallam) adati: “Iwo mwa inu amene amawerengera duruud kwambiri mu dunya adzakhala oyandikira kwa ine pa tsiku la Qiyaamah nthawi iliyonse. Munthu amene? Munthu amene angandiwelengere Durood Usiku ndi usana wa lachisanuJumuah, Mulungu adzamkwaniritsilira zosoweka zake kwa zana limodzi, zofunika makumi asanu ndi awiri za Aakhirah ndi zofunika makumi atatu za dunya. Duruud ikatha kuwerengedwa Allah amaipeleka kwa mngelo yemwe adzaibweretse mmanda ndikadzamwalira ngati mmene mphatso imaperekedwera kwa inu, mngelo amandidziwitsa za muntbu amene wapanga duruud dzina lake komanso la bambo ake ndipo kenako ndimaisamala.
Read More »Tafseer Ya Surah Qadr
بِسمِ اللّٰـهِ الرَّحمٰنِ الرَّحيمِ اِنَّا أَنزَلنٰهُ فى لَيْلَةِ القَدْرِ ﴿١﴾ وَما أَدرىٰكَ ما لَيلَةُ القَدرِ ﴿٢﴾ لَيلَةُ القَدرِ خَيرٌ مِن أَلفِ شَهرٍ ﴿٣﴾ تَنَزَّلُ المَلـٰئِكَةُ وَالرّوحُ فيها بِإِذنِ رَبِّهِم مِن كُلِّ أَمرٍ ﴿٤﴾ سَلـٰمٌ هِىَ حَتّىٰ مَطلَعِ الفَجرِ ﴿٥﴾ Ndithudi, Tayimvumbulutsa Qur’an mu usiku wa Qadr (olemekezeka kwambiri). Ndipo chingakudziwitse nchiyani za usiku olemekezeka kwambiriwu (Usiku wa qadar). Usiku …
Read More »Kupeza nawo chiombolo cha Mtumiki sallallahu alaih wasallam
عن رويفع بن الثابت قال: قال رسول الله صلى الله عليه وسلم: من صلى على محمد وقال: اللهم أنزله المقعد المقرب عندك يوم القيامة، وجبت له شفاعتي (المعجم الكبرى للطبراني، الرقم: 4480 ،وإسناده حسن كما في مجمع الزوائد، الرقم: 17304) Olemekezeka Ruwaifidh (radhiyallahu anhu) akufotokoza kuti, Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) …
Read More »Kuonjezereka kwa ma riziqi
عن سهل بن سعد رضي الله عنه قال: جاء رجل إلى النبي صلى الله عليه وسلم فشكا إليه الفقر وضيق العيش أو المعاش فقال له رسول الله صلى الله عليه وسلم: إذا دخلت منزلك فسلم إن كان فيه أحد أو لم يكن فيه أحد ثم سلم علي واقرأ قل هو …
Read More »Kuyankha Mawu A Iqaamah
Yankhani iqaama mofanana ngati mmene mumayankhira adhaan. Komabe pamene mukuyankha mawu awa قَدْ قَامَتِ الصَّلاَهْ (qad qaamatis salaah) mudzanena kuti:
Read More »Sawabu zofanana ndikupereka sadaqah ukawerenga Duruud
Olemekezeka Abu Sa'eed khudri (radhiyallahu anhu) akufotokoza kuti Mtumiki (sallallahu alaih wasallam) adati, "Msilamu amene alibe kena kalikonse kuti apereke sadaqah adziwerenga duruud iyi mkatikati mwa duwa yake popeza idzampezetsa iyeyo sawabu zoti wapeleka sadaqah ndikumuyeretsa ku machimo.
Read More »Mawu A Iqaamah Komanso Njira Ya Sunnat Yopangira Iqaamah
6. Tembenuzirani nkhope yanu kumanja pamene mukunena kuti: Hayya alas swalah ndiponso kumanzere pamene mukunena kuti: Hayya alaal falaah.[1] 7. Pamene Iqaamah yachitidwa musakhale otangwanika ndikupemphera swalati ya sunnah. Choncho kungotha iqaamah pompopompo yambani kupemphera ya faradh.[2] عن أبي هريرة رضي الله عنه عن النبي صلى الله عليه وسلم قال …
Read More »Sawabu zapaderadera ukawerenga Durood ka 100
عن أبي هريرة رضي الله عنه عن النبي صلى الله عليه وسلم قال من صلى علي عشرا صلى الله عليه مئة ومن صلى علي مئة صلى الله عليه ألفا ومن زاد صبابة وشوقا كنت له شفيعا وشهيدا يوم القيامة (أخرجه أبو موسى المديني بسند قال الشيخ مغلطاى لا بأس به، …
Read More »Mawu A Iqaamah Komanso Njira Ya Sunnat Yopangira Iqaamah
3. Pangani adhaan mofulumira poyankhula komanso motsitsa mawu.
Olemekezeka Jaabir (Radiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (salallahu alayhi wasallama (adamuuza Bilal (radhiyallahu anhu): Pamene ukupanga adhaan panga pang´onopang´ono (komanso uziima pambuyo powerenga mnzere uliwonse) Komano pamene ukupanga iqaamah ukuyenera upange mwachanguchangu."
Read More »