Adhaan Ndi Iqaamah

Mawu A Iqaamah Komanso Njira Ya Sunnat Yopangira Iqaamah

6. Tembenuzirani nkhope yanu kumanja pamene mukunena kuti: Hayya alas swalah ndiponso kumanzere pamene mukunena kuti: Hayya alaal falaah.[1] 7. Pamene Iqaamah yachitidwa musakhale otangwanika ndikupemphera swalati ya sunnah. Choncho kungotha iqaamah pompopompo yambani kupemphera ya faradh.[2] عن أبي هريرة رضي الله عنه عن النبي صلى الله عليه وسلم قال …

Read More »

Mawu A Iqaamah Komanso Njira Ya Sunnat Yopangira Iqaamah

3. Pangani adhaan mofulumira poyankhula komanso motsitsa mawu.

Olemekezeka Jaabir (Radiyallahu anhu) akusimba kuti Mtumiki (salallahu alayhi wasallama (adamuuza Bilal (radhiyallahu anhu): Pamene ukupanga adhaan panga pang´onopang´ono (komanso uziima pambuyo powerenga mnzere uliwonse) Komano pamene ukupanga iqaamah ukuyenera upange mwachanguchangu."

Read More »

Mawu A Iqaamah Komanso Njira Ya Sunnat Yopangira Iqaamah

1. Mawu a Iqaamah ndichimodzimodzi ndi azaana. Koma popanga iqaamah mukuyenera kunena kamodzikamodzi kupatula mawu onena kuti قد قامت الصلاة (Qadi qaamatis swalaah) mukuyenera kunena kawiri. Choncho mukatsiriza mawu oti Hayya alaal falaah mudzanena kuti: قَدْ قَامَتِ الصَّلَاةْ قَدْ قَامَتِ الصَّلَاةْ Qad qaamatis swalat, qad qaamatis swalaah (Swalah yaima swalah …

Read More »

Duwa Yonena Panthawi Ya Adhaana Ya Maghreb

Werengani duwa iyi pamene ikuchitika azaana ya maghreb kapena kutha kwa azaana yamaghreb.[1] اَللّٰهُمَّ إِنَّ هٰذَا إِقْبَالُ لَيْلِكَ وَإِدْبَارُ نَهَارِكَ وَأَصْوَاتُ دُعَاتِكَ فَاغْفِرْ لِيْ Oh Allah, Uku ndikufika kwa usiku ndiponso kuchoka kwa Usana ndiponso awa ndimawu oitana a akapolo anu (mamuadhin) choncho ndikhululukireni machimo anga. عن أم سلمة رضي …

Read More »

Duwa Kutha Kwa Azaana

2. Mukatsiriza kuwerenga duwa kutha kwa adhaana duwa iyinso mukuyenera kuwerengedwa. أَشْهَدُ أَنْ لَّا إِلٰهَ إِلَّا اللهُ وَحْدَهُ لَا شَرِيْكَ لَهُ وَأَنَّ مُحَمَّدًا عَبْدُهُ وَرَسُوْلُهُ رَضِيْتُ بِاللهِ رَبًّا وَبِمُحَمَّدٍ رَسُوْلًا وَبِالْإِسْلَامِ دِيْنًا Ndikuchitira Umboni kuti kulibe wina opembedzedwa mwachoonadi koma Allah yekha, Iye ndimmodzi yekha ndipo alibe ophatikizana naye. Ndiponso …

Read More »

Duwa Kutha Kwa Azaana

1. Ikatha Adhaan mukuyenera kuwerenga duruud pomufunira zabwino Mtumiki (sallallah alayhi wasallam).Pambuyo pake nenani duwa iyi:[1]  اَللّٰهُمَّ رَبَّ هٰذِهِ الدَّعْوَةِ التَّامَّةِ وَالصَّلَاةِ الْقَائِمَةِ آتِ مُحَمَّدًانِ الْوَسِيْلَةَ وَالْفَضِيْلَةَ وَابْعَثْهُ مَقَامًا مَّحْمُوْدًانِ الَّذِيْ وَعَدْتَّهُ إِنَّكَ لَاتُخْلِفُ الْمِيْعَادْ Oh Allah, Ndiinu Mbuye (mwini) wakuitana uku kwabwino kokwanilira ndiponso kuswala yomwe ili yopitilira. Mpatseni …

Read More »

Kuyankha Adhaan

Adhaan ndichizindikiro chachikulu chachisilamu. chifukwa choti adhaana ndichizindikiro chachikulu pachipembedzo chachisilamu tikuyenera kuonetsera ulemu ku adhaana ikamapangidwa poyankha, komanso ikamapangidwa osakhala otangwanika ndizinthu zamdziko lapansi. Ndipo sizofunikira pamene adhaana ikuchitika munthu kukhala otangwanika ndikuyankhula zinthu zamdziko lapansi.[1] 1) Pamene ikupangidwa adhaana, yankhani potsatizira mawu amene muadhini (opanga adhaana) akunena.[2] mwachitsanzo …

Read More »

Kapangidwe Ka Adhaan Ya Fajr/Subuhi

Ngati wina akupanga Adhaan ya fajr adzapanga monga zalongosoleredwera m’mbuyomu. kusiyana kudzangokhala koti akadzamaliza kunena mawu oti حي على الفلاح adzanena mawu:[1] اَلصَّلَاةُ خَيْرٌ مِّنَ النَّوْمْ Swalah ndi yabwino kuposa tulo. عن محمد بن عبد الملك بن أبي محذورة عن أبيه عن جده رضي الله عنه قال قلت يا رسول …

Read More »

Katchuridwe Koyenera Ka Mawu a Adhaan

Popanga Adhaan opangayo akuyenera kuwatchura mawu onse moyenera pachifukwa chimenechi pali mfundo zimene zikuyenera kutsatiridwa. 1. pamene mukuwerenga mawu oti راَللهُ أَكْبَرَ اللهُ أَكْبَرْ (raa) amene akupezeka pa أَكْبَرْ oyambilira mudzamuwerenga ndi fat-hah (ــَـ) mukamamulumikiza ndi liwu loti اَللهُ (Allahu). 2. mukamadzanena mawu oti أَشْهَدُ أَلَّا إِلٰهَ إِلَّا اللهْ liwu …

Read More »