Daily Archives: January 13, 2025

Olemekezeka Abdur Rahman bin Auf (Radhwiyallahu ‘anhu) ndi mmodzi mwa Asilamu opambana.

Nthawi ina Rasulullah (Swalla-Allaahu ‘alayhi wasallam) adamufunsa Busrah bint Safwan (Radhwiya-Allahu ‘anha) kuti ndi ndani amene ankafuna kukwatira mphwake, Umm Kulthuom bint Uqbah. Adamufotokozera mayina a anthu ochepa omwe adamfunsira mphwakeyo, ndipo adamuwuzanso kuti mwa anthu omwe adamfunsira mphwakeyo ndi Abdur Rahman bin Auf (Radhwiyallahu ‘anhu). Zitatero, Mtumiki (Swalla-Allaahu ‘alayhi …

Read More »