Olemekezeka Abu Zar (radhwiyallahu ‘anhu) atatsala pang’ono kumwalira, panalibe wina aliyense kupatula mkazi wake ndi kapolo wake. Anawalangiza kuti, “Mundisambitse ndi kundiveka sanda (ndikamwalira). Kenako tengani thupi langa ndi kuliyika pamsewu. Uzani gulu la anthu lomwe liyambilire kudutsa kuti, “Uyu ndi Abu Zar (radhwiyallahu ‘anhu),Otsatira wa Rasulullah (swallallahu ‘alayhi wasallam). …
Read More »Yearly Archives: 2025
kupezeka Kwa Chilungamo ndi Madalitso Mkatikati mwa Ulamuliro wa Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu)
Ulamuliro wa Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu) udzakhala wa chilungamo ndi barakah (madalitso). Popeza Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu) adzasankhidwa ndi Allah Ta‘ala kuti autsogolere ummah isadafike Qiyaamah, adzatsogozedwa ndi Allah ndikuthandizidwa ndi Iye. Popeza, chisankho chilichonse chomwe adzachite chidzadzazidwa ndi zabwino ndi chilungamo. Nthawi ya ulamuliro wake, Allah Ta‘ala adzadalitsa Asilamu ndi ma …
Read More »Olemekezeka Abu Zarr adzudzula wantchito wake
Tsiku lina munthu ochokera ku fuko la Banu Sulaim anabwera kwa Abu Zarr (radhwiyallahu anhu) ndipo anamuuza kuti: “Ndikufuna kukhala nanu kuti ndipindule ndi maphunziro anu a malamulo a Allah Ta’ala ndi ma sunnah a Nabi swallallahu alaihi wasallam Inenso ndidzathandiza wantchito wanu kusamalira ngamila.” Abu Zarr radhwiyallahu anhu anayankha …
Read More »Sunnats Ndi Aadaab Za Mwezi Wa Zul Hijjah
1. Mulimbikire kuchita ibaadah m’masiku khumi oyambirira a Zul Hijjah. Malipiro aakulu atchulidwa pa ibaadah yomwe ingachitike m’masiku khumi amenewa. Olemekezeka Abdullah bin Abbaas radhwiyallahu anhu wanena kuti Nabiy swallallahu alaihi wasallam adati: “Palibe cholungama chomwe chingachitike tsiku lililonse la chaka chomwe chili chabwino kwambiri kuposa masiku khumi a mwezi …
Read More »Abu Zarr (radhwiyallahu ‘anhu) Alemekeza kwambiri Uthmaan (radhwiyallahu ‘anhu)
Munthu wina ochokera ku fuko la Banu Sulaym adayankhula izi: “Nthawi ina ndinakhala pa gulu lomwe Abu Zarr anali pomwepo. Maganizo anga anali oti mwina Abu Zarr wamukwiyira Uthmaan (radhwiyallahu ‘anhu) chifukwa choti Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu) adamupempha kuti asamuke ku Madinah Munawwarah ndikukakhala ku Rabadha. Pagulupo wina adapereka ndemanga yomutsutsa …
Read More »Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu)
Kubwera kwa Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu) ndi chizindikiro choyamba mwa zizindikiro zikuluzikulu zomwe zidzawonekere Qiyaamah isadafike. M’mahadith odalitsika ambiri, Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam) adalosera za kubwera kwa Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu) ku ummah uno. Allaamah Suyuuti (rahimahullah) wafotokoza kuti mahadith okhudzana ndi kubwera kwa Mahdi (radhwiyallahu ‘anhu) ndi ochuluka kwambiri kotero kuti …
Read More »Zul Hijjah
Mwezi wa Zul Hijjah uli mgulu la miyezi inayi yopatulika ya kalendala ya Chisilamu. Miyezi inayi yopatulika imeneyi ndi Zul Qa’dah, Zul Hijjah, Muharram ndi Rajab. Malipiro a ntchito zabwino zochitidwa m’miyezi imeneyi amachulukitsidwa, ndipo machimo amene achitidwa m’miyezi imeneyi nawonso amatengedwa kuti ndi oipitsitsa kwambiri. Allah Ta’ala akuti: إِنَّ …
Read More »Olemekezeka Abu Zarr (radhwiyallahu ‘anhu) asamukira ku Shaam ndi Rabadhah
Zidatengera Abu Zarr Ghifaari (radhiyallahu ‘anhu) kuphunzira moyo wa Rasulullah (sallallahu ‘alaihi wasallam) osasamala za moyo wadziko lapansi komanso kudziletsa ndi kumvera machenjezo amphamvu kwa omwe ali ndi chuma koma osagwiritsa ntchito moyenera, Abu Zarr (radhwiyallahu ‘anhu) adayamba kudana ndi dziko lapansi kotero kuti sanasunge chuma ndipo sankakonda kuona anthu …
Read More »Ma Sunnah Komanso Miyambo Ya Jumu’ah 4
11. Werengani durood mochuluka. Olemekezeka Aws bin Aws radhwiyallahu anhu akufotokoza kuti Mtumiki (swallallahu alaihi wasallam) adati: “Masiku abwino kwambiri ndi tsiku la Jumuah. 12. Yesetsani kuwerenga duruud chikwi chimodzi (ka 1000) tsiku la Jumuah. Olemekezeka Anas radhwiyallahu anhu akusimba kuti Mtumiki swallallahu alaihi wasallam adati: “Amene amawerenga duruud pa …
Read More »Kusalilabadira kwa Abu Zar (radhwiyallahu ‘anhu) Ddziko Lapansi
Abu Zar Ghifaari (Radhwiyallahu ‘anhu) anali Sahaabi yemwe ankafanana ndi Nabiy Isa (‘alaihis salaam) m’maonekedwe ake komanso kukongola kwake. Rasulullah (sallallahu ‘alaihi wasallam) anati, “Aliyense amene akufuna kumuona Isa bin Maryam (‘alaihis salaam) Taqwa yake, chilungamo chake, ndi kudzipereka kwake (pa ibaadah), ayenera kumuyang’ana Abu Zar” (Majmauz Zawaaid #15817) Chimodzimodzinso, …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu