16.Lekani kulongosora mwatsatanetsatane pa dua yanu. M’malo mwake, muyenera kupempha zabwino zonse. Nthawi ina Abdullah bin Mughaffal Radhwiyallahu anhu anamva mwana wake akupempha m’mawu otsatirawa: “O Allah! Ndikukupemphani nyumba yachifumu yoyera kumbali yakumanja kwa Jannah ndikalowa m’menemo.” Atamva izi Abdullah bin Mughaffal (Radhwiyallahu anhu) adati: “E, mwana wanga! Mpemphe Allah …
Read More »Monthly Archives: December 2024
Olemekezeka Talhah (Radhiyallahu ‘anhu) pa Nkhondo ya Uhud
Olemekezeka Jaabir bin Abdillah (Radhwiya Allaahu ‘anhu) adati: Pa tsiku la nkhkndo ya Uhud, pamene ma Swahaabah adayamba kuthawa kunkhondo, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) adasiidwa yekha pamalo ena ndi ma Swahaaba khumi ndi awiri okha.) Ma mushrikiin atapita kwa Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) ndi ma Swahaabah khumi ndi …
Read More »