Abu Muslim Khowlaani (rahimahullah) akufotokoza kuti: “Ndinalowa mumzikiti wa Hims ndipo ndinaona gulu la anthu. Pakati pawo panali anzake makumi atatu ndi awiri a Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) omwe ankakambirana za mahadith kuchokera kwa Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam). Munkumanowu munali mnyamata, amene maso ake anali atapakidwa surma ndipo mano ake …
Read More »Monthly Archives: July 2026
Sunnati Ndi Adaab 3
12. Ngati mungadzukire pakati pa usiku, werengani dua yotsatirayi ya masnun ndipo pambuyo pake mutha kupempha kwa Allah Talaa. Insha Allah, dua yanu idzalandiridwa. لَا إِلٰهَ إِلَّا اللهُ وَحْدَهُ لَا شَرِيْكَ لَهُ لَهُ الْمُلْكُ وَلَهُ الْحَمْدُ وَهُوَ عَلٰى كُلِّ شَيْءٍ قَدِيْرْ اَلْحَمْدُ لِلّٰهِ وَسُبْحَانَ اللهِ وَلَا إِلٰهَ إِلَّا اللهُ وَاللهُ …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu