Nkhani yotsatirayi ikuunikira kumvetsetsa kwakuya kwa dini ndi ma’rifat (kuzindikirika) ya Allah Talaa zomwe Allah Talaa adamudalitsa nazo Bishr Haafi (rahimahulla) zomwe zidachititsa kuti mpaka Imam Ahmad (rahimahulla) amutsanzire: M’nthawi ya Imaam Ahmad bin Hambal (rahimahulla) kunali dotolo wina yemwe ankatchedwa kuti Abdur Rahmaan At-Tabeeb. Ankathandiza Imaam Ahmad bin Hambal …
Read More »Monthly Archives: June 2026
Chikondi cha Rasulullah (Sallallahu ‘alaihi wasallam) kwa Sayyiduna Muaaz bin Jabal (radhiwyallahu ‘anhu)
Sayyiduna Muaaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu) akunena kuti nthawi ina, Nabi (Swallallahu alaihi wasallam) anagwira dzanja langa nati kwa ine, “O Muaaz!”, ndipo ine ndinayankha kuti, “Ndili pano kuti ndikutumikireni.” Rasulullah (Swallallahu alaihi wasallam) kenako anandiuza kuti, “Ndithudi, ndimakukonda (chifukwa cha Allah Ta’ala).” Muaaz bin Jabal (Radhwiyallahu ‘anhu) anayankha kuti, …
Read More »Muaaz (radhwiyallahu ‘anhu) Aswa fano la Amr bin Jamuuh (radhwiyallahu ‘anhu)
M’chaka cha 13 cha nubuwwat, anthu 70 ochokera ku Ansaar anabwera ku Hajj ndipo analowa Chisilamu pamaso pa Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam). Pakati pawo panali Muaaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu) yemwe anali ochokera ku fuko la Banu Salimah la Ansaar, ndipo anali m’gulu la anthu oyambilira ku fuko lawo kulowa …
Read More »Kupereka kwa Mu’aaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu)
Nthawi ina,Olemekezeka Umar (radhwiyallahu ‘anhu) anatumiza ndalama zagolide mazana anayi kwa Abu ‘Ubaidah bin Jarraah (radhwiyallahu ‘anhu) ndipo analamula mthumwiyi kuti ikadikire pang’ono kuti aone zomwe achite nacho chumacho. Olemekezeka Abu Ubaydah (radhwiyallahu ‘anhu) atalandira ndalamazo, anati, “Allah amuchitire chifundo (kunena Umar).” Kenako anauza kapolo wake wamkazi kuti, “Tenga ndalama …
Read More »Nkhondo Yaikulu ndi Kugonjetsedwa kwa Istanbul
Mahdi atabwera, Allah Ta‘ala adzawapatsa Asilamu uysogoleri ndi mphamvu padziko lonse lapansi. Akristu adzazindikira kuti Asilamu akupeza thandizo ndipo akukula mphamvu tsiku ndi tsiku. Kenako adzakonza gulu lankhondo lalikulu kuti amenyane ndi Mahdi ndi Asilamu. Zanenedwa mu Hadith kuti Akristu ochokera m’maiko onse adzasonkhanitsa asilikali awo ndikukonzekera kumenyana ndi Asilamu. …
Read More »Sunnati Ndi Adaab 2
6. Pangani ma dua komanso azkaar musanagone; اللَّهُمَّ بِاسْمِكَ أَمُوْتُ وَأَحْيٰ O, Allah Talaa mdzina Lanu ndikufa komanso ndiuka 7. Gonerani kumanja ndikuika dzanja lanu lamanja pansi pa tsaya lanu lakumanja. Bibi Hafsah (radiyallahu anha) akusimba kuti Mtumiki (Swallallahu alaihi wasallam) akafuna kugona, ankaika dzanja lake lamanja pansi pa tsaya …
Read More »Munthu Olungama Kwambiri – Fudhail Bin Iyaaz Rahimahullah
Fudhail bun Iyaaz (Rahimahullah) aDali Muhaddith olemekezeka komanso oyera mtima wa m’nthawi yake. Allah Talaa adamdalitsa ndi ulemelero wapamwamba kwambiri mu Hadith kotero kuti ambiri mwa ma Muhadith otsogola, monga Abdullah bin Mubaarak, Sufyaan bun Uyainah ndi Imaam Shaafi’e (Rahimahullah) adafotokoza Hadith kuchokera kwa iye. Zanenedwa kuti Fudhail (Rahimahullah) asanadalitsidwe …
Read More »Rasulullah (Swallallahu ‘alaihi wasallam) Amuitana Abdullah bin Mas’ud (radhwiyallahu ‘anhu) ku Moyo Osatha
Salamah bin Tammaam (rahimahullah) akufotokoza kuti: Masiku angapo Abdullah bin Mas’ud (radhiyallahu ‘anhu) asanamwalire, munthu wina adabwera kudzakumana naye. Atakumana naye, munthuyo anamuuza kuti, “Oh Ibnu Mas’ud! Usiku watha, ndinakulota. M’maloto, ndinamuona Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) atakhala pa guwa pomwe iwe unali pansi pake. “Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) anakulankhula nanu …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu