Daily Archives: July 6, 2026

Kudziwa Kwambiri Dini kwa Muaaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu)

Abu Muslim Khowlaani (rahimahullah) akufotokoza kuti: “Ndinalowa mumzikiti wa Hims ndipo ndinaona gulu la anthu. Pakati pawo panali anzake makumi atatu ndi awiri a Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) omwe ankakambirana za mahadith kuchokera kwa Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam). Munkumanowu munali mnyamata, amene maso ake anali atapakidwa surma ndipo mano ake …

Read More »