Misampha iwiri ikuluikulu ya shaitaan yosocheretsera munthu ndi chuma ndi akazi. Misampha iwiriyi ndi yowononga kwambiri. Ndipo machimo ambiri omwe amachitika padziko lapansi amachokera ku misampha iwiriyi. Rasulullah adati “Ndithudi, dziko lapansi ndi lokoma komanso lokongola ( lokongola komanso lokopa) ndipo Allah Talaa wakusankhani kukhala oimira padziko lapansi, kuti ayang’ane …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu