Daily Archives: October 5, 2026

Olemekezeka Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) Athandiza Munthu Osauka Kukwatira Mwana Wake Wamkazi

Nthawi ina, gulu la ma Qurraa (omwe anali akatswiri powerenga Qur’aan Majiid) ochokera ku Basrah anabwera kwa Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) ndipo anamuuza kuti, “Pali munthu opembedza amene amakhala m’dera lathu, amene nthawi zambiri amasala kudya ndi kuchita Tahajjud kwambiri. Ndi opembedza kwambiri kotero kuti aliyense wa ife amamusilira …

Read More »