Chisilamu chidapereka malamulo ndi ziletso, ma sunnah ndi aadaab (miyambo yabwino), kuti ziphunzitse munthu momwe angakhalire muzochitika ndi makhalidwe onse. Monga momwe dini ya Chisilamu yaperekera chitsogozo kwa munthu akakhala pakhomo, yapereka chitsogozo cha momwe ayenera kuchitira akakhala pa paulendo (ulendo). Mu kuyankhula kwina, dini ya Chisilamu ndi yatsatanetsatane, yokwanira …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu