Daily Archives: November 9, 2026

Kuloweza modabwitsa kwa Abu Hurairah (Radhwiyallahu ‘anhu) – Zotsatira za Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wa aalihi wa sallam) Kunena Aameen ku Dua Yake.

Munthu wina adadza kwa Zaid bin Thaabit (Radhwiyallahu ‘anhu) kuti adzafunse za malamulo dini. Zaid (Radhwiyallahu ‘anhu) adamutumiza kwa Abu Hurairah (Radhwiyallahu ‘anhu). Kenako Zaid (Radhwiya Allaahu ‘anhu) adati kwa munthuyo: Nthawi ina ndidali munzikiti ndi Abu Hurairah ndi Sahaabi wina, ndikupemphera ndikukumbukira Allah Ta’ala. Rasulullah (Swalla Allaahu ‘alayhi wa …

Read More »