Daily Archives: October 19, 2024

Zizindikiro za Qiyaamah 2

Cholinga Choufotokozera Ummah Zizindikiro za Qiyaamah Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) adaufotokozera Ummah za zisonyezo zing’onozing’ono ndi zikuluzikulu zomwe zidzaonekere Qiyaamah isanabwere. Zambiri mwa zizindikiro zing’onozing’ono zakhala zikuonekera kale m’zaka mazana ambiri zapitazo, pamene zambiri mwa zizindikirozi zikuchitiridwa umboni lerolino. Aalim wina yemwenso ndi Muhaddith, Allaamah Qurtubi (rahimahullah), watchula zifukwa …

Read More »