Monthly Archives: October 2024

Kuopa Allah Taala

Qataadah (Rahimahullah) akusimba kuti Olemekezeka Abu Ubaidah (Radhwiyallahu ‘anhu) ankati, (chifukwa choopa kudzaima pamaso pa Allah Ta’ala pa tsiku la Qiyamah ndi kuwerengetsedwa ntchito zake. وددت أني كنت كبشا، فيذبحني أهلي، فيأكلون لحمي، ويحسون مرقي. “Ndikulakalaka ndikadakhala nkhosa. Ondipha akadandipha, akanadya nyama yanga ndikumwa nsuzi wanga. (Siyaru Aa’laamin Nubalaa 3/14) …

Read More »

Ntendere Waukulu Wa Allah Pa Akapolo Ndi Kukhala Makolo

Ena mwa madaritso aukuluakulu a Mulungu pa munthu, ndi mdaritso okhala ndi makolo. Mwayi okhalandi makolo ndi mdaritso ofunika kwambiri ndipo ulibe mlowa m’malo komanso umaperekedwa kwa munthu kamodzi kokha m’moyo wake. Monga momwe chisomo cha kukhala ndi moyo chimaperekedwa kamodzi kokha kwa munthu, ndipo chikatha sichidzabwereranso, momwemonso chisomo chokhala …

Read More »