Daily Archives: May 12, 2025

Sayyiduna Sa’iid Ibn Zaid (Radhwiyallahu ‘anhu) Ayikidwa m’gulu la Otenga nawo gawo pa nkhondo ya Badr

Nkhondo ya Badr isanayambike, Mtumiki (Swalla Allaahu ‘alayhi wasallam) atamva kuti gulu la ochita malonda la Ma Quraish, lolemedwa ndi chuma chawo, lachoka ku Shaam (Syria) ndipo likubwerera ku Makkah Mukarramah, adatumiza Talhah bin Ubaidullah ndi Sa’iid radhwiyallahu anhuma kuti akasonkhanitse uthenga okhudza Gululi. Izi zidachitika masiku khumi Rasulullah (Swalla …

Read More »