4. Mukamayendera odwala, pemphani dua iyi: لا بَأْسَ طَهُورٌ إِنْ شَاءَ اللهُ Palibe chifukwa chodera nkhawa, insha-Allah kudzera mu matendawa, muyeretsedwa. Mukhozanso kubwereza dua iyi kasanu ndi kawiri: أَسْأَلُ اللهَ الْعَظِيمَ رَبَّ الْعَرْشِ الْعَظِيمِ أَنْ يُشْفِيكَ Ndikumupempha Allah Wamphamvu zoposa, Mbuye wa Mpando Wachifumu waukulu, kuti akuchizeni. عن ابن عباس …
Read More »Monthly Archives: April 2025
Sayyiduna ‘Abdur Rahmaan bin ‘Auf (Radhiyallahu ‘anhu) apatsidwa Udindo osankha Khalifah.
Pambuyo pake, Sayyiduna “Umar (radhiyallahu ‘anhu) adapanga Shura (gulu la akuluakulu omwe azipanga ziganizo) lokhala ndi ma Swahaabah asanu ndi mmodzi otsatirawa: Ali (radhiyallahu ‘anhu), ‘Uthmaan (radhiyallahu ‘anhu), Zubair (radhiyah ‘anhu) Sa’d (Radhiyallahu ‘anhu) ndi Abdur Rahmaan bun ‘Auf (radhiyallahu ‘anhu). Pankhani ya ma Sahaabah asanu ndi mmodziwa (Radhiyallahu ‘anhum), …
Read More »Ma Sunnah Komanso Miyambo Yokaonera Odwala
1. Ndi mustahab (zofunika kwambiri) kupanga wudhu usanakamuyendere odwala.[1] Olemekezeka Anas Radhwiyallahu anhu akusimba kuti Rasulullah swallallahu alaihi wasallam adati; “Amene wapanga wudhu wangwiro (pokwaniritsa masunnah ndi ma mustahab onse a wudhu) ndi kupita kukacheza ndi m’bale wake wachisilamu yemwe akudwala ndi chiyembekezo cholandira malipiro oyendera odwala, munthu oteroyo adzaikidwa …
Read More »Kuopa kwa Olemekezeka Abdur Rahman bin Auf (radhiyallahu ‘anhu) kufunsidwa
Naufal bin lyaas al Huzali (rahimahullah) adati: ‘Tikakhala pamodzi ndi Abdur Rahman bin Auf (Radhwiyallahu ‘anhu), ndi kukhala naye chifupi kodabwitsa kusangalatsirenji. Tsiku lina, anatitengera kunyumba kwake kuti tikadye, Titakhala pansi kuti tidye ndipo mbale ya chakudya ya nyama ndi mkate inaperekedwa pamaso pathu, iye adayamba kulira. Tidamufunsa: “Nchiyani chikukupangitsa …
Read More »Maonekedwe a chithupithupi cha Dajjaal
M’mahadithi olemekezeka, Olekezeka Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam) adatsimikizira ummah za Maonekedwe a Dajjaal a umunthu. Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam) kufotokoza za Dajjaal m’maonekedwe a munthu zikuonetsa kuti Dajjaal ndi munthu. Pa chifukwa chimenechi, chikhulupiriro cha Ahlus Sunnah wal Jamaa’ah ndi chakuti Dajjaal ndi munthu, ndipo adzabwera pa dziko lapansi nthawi …
Read More »Kulandira Uthenga Wabwino Wamwayi Ndi Chikhululukiro M’maloto
Usiku wina, Hazrat Abdur Rahmaan bin Auf (Radhwiyallahu ‘anhu) adakomoka kwa nthawi yayitali chifukwa chakudwala kwake mpaka omwe anali pafupi naye adaganiza kuti mzimu wake wachoka. Anamuphimba ndi nsalu n’kuchokapo. Mkazi wake, Ummu Kulthum bint ‘Uqbah, nthawi yomweyo adapempha thandizo kwa Allah Ta’ala podekha ndi kuswali (monga talamulidwa kutero mu …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu