Kuti dziko liziyenda bwino komanso mogwirizana, ndikofunikira kuti munthu aliyense alemekeze ufulu wa anthu ena. Ngati ufulu wa anthu siulemekezedwa ndi kukwaniritsidwa, ndiye kuti chisokonezo ndi mikangano zidzafalikira padziko lonse lapansi. Kuba ndi kulanda chuma kudzakhala paliponse ndipo kuponderezana ndi kuphwanya malamulo kudzakhala chinthu chotchuka kwambiri. Anthu adzapondereza ufulu wa …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu