Mu’aaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu) akunena kuti, “Nthawi ina, ndinali nditakhala kumbuyo kwa Rasulullah (sallallahu ‘alaihi wasallam) pa bulu pamene naye analinso pomwepo. Panalibe chilichonse pakati pa ine ndi Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam) kupatula thabwa la chokhalira (chomwe chimalekanitsa okwera ndi munthu amene wakhala kumbuyo kwake). “Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu