Daily Archives: August 3, 2026

Malangizo Osiyanirana a Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam) kwa Mu’aaz (radhwiyallahu ‘anhu) pamene ankamutumiza ku Yemen

Pamene Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) ankatumiza Mu’aaz bin Jabal (radhwiyallahu ‘anhu) ku Yemen kuti akaphunzitse anthu dini ndikuwalamulira, posiyana naye, Rasulullah (swallallahu ‘alaihi wasallam) ankayenda naye mpaka kunja kwa mzinda wa Madinah Munawwarah pamene ankamupatsa uphungu osiyanirana. Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) anamulamula kuti achite zinthu zina zabwino, ndipo anamulamula kuti …

Read More »