Munthu wina anabwera kwa Hazrat Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) atalowa i’tikaaf mu Masjid ya Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam). Munthuyo anamulonjera ndi salaam kenako anakhala pansi. Hazrat Abdullah bin Abbas (radhwiyallahu ‘anhuma) adati kwa iye: “Ndikuona kuti ndiiwe okhumudwa.” Munthuyo anayankha kuti, “Inde, oh msuweni wa Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam). …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu