Salaah Ya Amuna

Qa’dah ndi Salaam

9. Osatsitsa kapena kugwedeza mutu pamene mukupanga salaamu. 10. Tembenuzirani nkhope yanu mbali zonse ziwiri moti amene ali m’mbuyo mwanu athe kuona tsaya lanu.[1] 11. Werengani mawu oti اَسْتَغْفِرُ الله katatu pambuyo pa salaam.[2] 12. Pangani ma dua popeza iyi ndi nthawi yoyankhidwa ma dua.[2] 13. Werengani Tasbeeh Faatimi kutha …

Read More »

Qa’dah ndi Salaam

5. Ngati ukuswali rakaah zitatu kapena zinayi kenako ukamaliza kuwerenga tashahhud m’qa’dah yoyamba, nawenso werenga swalaah alan Nabi (durood). Powerenga Swala ya alan Nabi (durood), اللهم صل على محمد  werengani mpaka dzina lodalitsika la Mtumiki (swallallahu alaih wasallam) Kenako imirirani rakaah yachitatu. Musapange dua pambuyo powerenga Swalaat alan Nabi (durood).[1] …

Read More »

Qa’dah ndi Salaam

1. Pambuyo pa sajda yachiwiri ya rakaah yachiwiri, khalani tawarruk kutanthauza kukhala ndi thako lakumanzere ndikutulutsa phazi lakumanzere pansi pa mwendo wakumanja. Phazi lakumanja likhale lowongoka ndi zala ziyang’ane kuchibla. Chidziwitso : Kukhala m’malo a tawarruk kumagwiranso ntchito pa swala yomwe ili ndi qa’dah imodzi mwachitsanzo rakaah ziwiri ndi qa’dah …

Read More »

Rakaah Yachiwiri

1. Mukamanyamuka pa sajdah, choyamba nyamulani chipumi ndi mphuno, kenako zikhato ndikumalizira mawondo. 2. Pamene mukuimirira Rakah yachiwiri, tsamizirani manja anu pansi uku mukuimilira.[1] 3. Pitirizani rakaah yachiwiri monga mwachizolowezi (kupatula Dua-ul Istiftaah simudzaiwerenga).[2] [1] وإذا أراد القيام من السجود أو الجلوس اعتمد بيديه معا على الأرض ونهض ولا أحب …

Read More »

jalsah

6. Iwerengeninso dua iyi pamene muli Pa Jalsah:[1] اللَّهُمَّ اغْفِرْ لِي، وَارْحَمْنِي، وَعَافِنِي، وَاجْبُرْنِي، وَارْفَعْنِي، وَاهْدِنِي، وَارْزُقْنِي Oh Allah, ndikhululukireni, ndichitireni chifundo, ndichotsereni kufooka kwanga, ndikwezeni pa udindo, ndiongolereni ndi kundidalitsa ndi riziki. 7. Nenani takbira ndipo pitirirani ku sajda yachiwiri monga mwachizolowezi.[2] 8. Imirirani kuchokera pa sajdah yachiwiri nkukhala …

Read More »

Sajdah

12. Werengani Takbiir ndikukhala pansi mukachoka pa Sajdah yoyamba, imeneyi imatchedwa kuti I’tidaal.[1] Jalsah 1. Mukukhala kwanu pa jalsah, ikani manja anu pa ntchafu zanu ndi zala zanu pafupi ndi mawondo anu.[2] 2. Gwirizanitsani zala zanu.[3] 3. Yang’anani malo a Sajdah uku muli pa Jalsah.[4] 4. Phazi lakumanja likhale lolunjika …

Read More »

Sajdah

7. Asungeni manja anu M’mbali.[1] 8. Yang’anani pa malo a Sajdah.[2] 9. Sungani mpata pakati pa mimba ndi ntchafu.[3] 10. Miyendo yonse iwiri ikhale pansi ndi zala zammiyendo zitaloza ku chibla. Sungani mpata wa dzanja limodzi pakati pa mapazi anu pa sajdah.[4] 11. Werengani katatu kapena nambala yosagawika ndi 2 …

Read More »

Sajdah

1. Nenani takbira, ndipo popanda kukweza manja anu, pitani pa sajdah.[1] 2. Gwirani manja m’maondo uku mukupita pa Sajdah.[2] 3. Yambani ndikuika mawondo pansi, kenako manja, ndipo pomalizira pake Ikani chipumi ndi mphuno pamodzi.[3] 4. Ikani zikhatho pansi m’njira yoti zala zifanane ndi makutu ndipo mbali zapansi zigwirizane ndi mapewa.[4] …

Read More »

Ruku Ndi I’tidaal

6. Onetsetsani kuti manja asungidwa kutali ndi thupi.[1] 7. Lankhulani katatu kapena nambala yosagawanikana.[2] سُبْحَانَ رَبِّيَ الْعَظِيمِ Walemekezeka Mbuye wanga, Wamkulukulu. 8. Pambuyo powerenga tasbeeh, imirirani kuchokera ku rukuu uku mukunena tasmee:[3] سَمِعَ اللهُ لِمَنْ حَمِدَهُ Mulungu amamva amene Wamtamanda. 9.Kwezani manja (monga momwe tafotokozera mu takbeeratul ihraam) ndipo ikani …

Read More »

Ruku Ndi I’tidaal

1. Mukamaliza kuwerenga Surah Faatihah ndi surah ina, yimani kaye pang’ono ndipo kenako kwezani manja anu (monga momwe tafotokozera mu takbeeratul ihraam) uku mukunena takbira ndi kupita pa rukuu.”[1] Zindikirani: Takbeeraat intiqaaliyyah (takbira yomwe imanenedwa posuntha kuchoka ku kaimidwe kena kupita ku kena) iyenera kuyambika munthu akangoyamba kusuntha kupita ku …

Read More »