Yearly Archives: 2022

Kuyankha Adhaan

Adhaan ndichizindikiro chachikulu chachisilamu. chifukwa choti adhaana ndichizindikiro chachikulu pachipembedzo chachisilamu tikuyenera kuonetsera ulemu ku adhaana ikamapangidwa poyankha, komanso ikamapangidwa osakhala otangwanika ndizinthu zamdziko lapansi. Ndipo sizofunikira pamene adhaana ikuchitika munthu kukhala otangwanika ndikuyankhula zinthu zamdziko lapansi.[1] 1) Pamene ikupangidwa adhaana, yankhani potsatizira mawu amene muadhini (opanga adhaana) akunena.[2] mwachitsanzo …

Read More »

Tafseer Ya Surah Teen

وَالتِّينِ وَالزَّيْتُونِ ﴿١﴾ وَطُورِ سِينِينَ ﴿٢﴾ وَهَـٰذَا الْبَلَدِ الْأَمِينِ ﴿٣﴾ لَقَدْ خَلَقْنَا الْإِنسَانَ فِي أَحْسَنِ تَقْوِيمٍ ﴿٤﴾ ثُمَّ رَدَدْنَاهُ أَسْفَلَ سَافِلِينَ ﴿٥﴾ إِلَّا الَّذِينَ آمَنُوا وَعَمِلُوا الصَّالِحَاتِ فَلَهُمْ أَجْرٌ غَيْرُ مَمْنُونٍ ﴿٦﴾ فَمَا يُكَذِّبُكَ بَعْدُ بِالدِّينِ ﴿٧﴾ أَلَيْسَ اللّٰـهُ بِاَحْكَمِ الْحَاكِمِينَ ﴿٨﴾ Ndikulumbilira mitengo ya Mkuyu ndi Zitona, ndikulumbiliranso phiri la Sinai, …

Read More »

Kapangidwe Ka Adhaan Ya Fajr/Subuhi

Ngati wina akupanga Adhaan ya fajr adzapanga monga zalongosoleredwera m’mbuyomu. kusiyana kudzangokhala koti akadzamaliza kunena mawu oti حي على الفلاح adzanena mawu:[1] اَلصَّلَاةُ خَيْرٌ مِّنَ النَّوْمْ Swalah ndi yabwino kuposa tulo. عن محمد بن عبد الملك بن أبي محذورة عن أبيه عن جده رضي الله عنه قال قلت يا رسول …

Read More »

Kupeza Sawabu Zokwana Qeeraat Imodzi

عن علي بن أبي طالب رضي الله عنه أن رسول الله صلى الله عليه وسلم قال : من صلى علي صلاة كتب الله له قيراطا والقيراط مثل أحد (مصنف عبد الرزاق، الرقم: 153، وسنده ضعيف كما في القول البديع صـ 260) Sayyiduna Aliy bin Abi Taalib radhiyallahu anhu akufotokoza kuti …

Read More »

Katchuridwe Koyenera Ka Mawu a Adhaan

Popanga Adhaan opangayo akuyenera kuwatchura mawu onse moyenera pachifukwa chimenechi pali mfundo zimene zikuyenera kutsatiridwa. 1. pamene mukuwerenga mawu oti راَللهُ أَكْبَرَ اللهُ أَكْبَرْ (raa) amene akupezeka pa أَكْبَرْ oyambilira mudzamuwerenga ndi fat-hah (ــَـ) mukamamulumikiza ndi liwu loti اَللهُ (Allahu). 2. mukamadzanena mawu oti أَشْهَدُ أَلَّا إِلٰهَ إِلَّا اللهْ liwu …

Read More »

Mawu a Adhaan

Mu Adhaan muli magawo amawu okwana asanu ndi awiri, mawu asanu ndi awiriwa atchulidwa mmusimu:[1] 1. Poyamba mudzanena mawu awa: اَللهُ أَكْبَرَ اللهُ أَكْبَرْ Allah ndi wankulu, Allah ndi wankulu اَللهُ أَكْبَرَ اللهُ أَكْبَرْ Allah ndi wankulu, Allah ndi wankulu 2. Pachiwiripa mudzanena mawu anayi awa koma mudzayamba ndikunena motsitsa …

Read More »

Tafseer Ya Surah Inshiraah

أَلَمْ نَشْرَحْ لَكَ صَدْرَكَ ﴿١﴾ وَوَضَعْنَا عَنكَ وِزْرَكَ ﴿٢﴾ الَّذِي أَنقَضَ ظَهْرَكَ ﴿٣﴾وَرَفَعْنَا لَكَ ذِكْرَكَ ﴿٤﴾ فَإِنَّ مَعَ الْعُسْرِ يُسْرًا ﴿٥﴾ إِنَّ مَعَ الْعُسْرِ يُسْرًا ﴿٦﴾ فَإِذَا فَرَغْتَ فَانصَبْ ﴿٧﴾ وَإِلَىٰ رَبِّكَ فَارْغَب. Kodi sitidatsegule chidali chako (pokupatsa chikhulupiliro, chiongoko ndi nzeru zochuluka). Ndipo takuchotsera ntolo wako (pa tchito yolalikira …

Read More »