Daily Archives: July 5, 2025

Zida Zikuluzikulu za Dajjaal – Chuma, Akazi ndi Zansangulutso

Dajjaal akadzaonekera padziko, zida zikuluzikulu zomwe adzagwiritse ntchito kusocheretsera munthu ndi chuma, akazi ndi zansangulutso. Allah Ta’ala adzamupatsa mphamvu yochita zozizwitsa kotero kuti onse amene azidzaziona adzakopeka ndi kutengeka ndi fitnah (Mayesero) ake. Allah Ta’ala adzamloleza kugwetsa mvula, kupangitsa nthaka kutulutsa mbewu, ndipo chuma cha m’nthaka chidzamtsatira kulikonse kumene azidzapita. …

Read More »