Daily Archives: April 13, 2026

Hazrat Abdullah ibn Mas’uud (radhiyallahu anhu) Kuwerenga Qur’aan Majeed mokweza mawu pamaso pa Aquraish

Hazrat Abdullah ibn Mas’uud (radhiyallahu anhu) adali munthu oyamba kuwerenga Qur’aan Majeed mokweza mawu ku Makkah Mukarramah Aquraish asanalowe Chisilamu. Tsiku lina, maSwahaabah (radhiyallahu anhum) anasonkhana nati, “Ndikulumbira mwa Allah, Aquraish sanamvepo wina akuwerenga Qur’aan mokweza mawu pamaso pawo, ndiye ndani pakati pathu amene ali okonzeka kupita kukawerenga Qur’aan mokweza …

Read More »