Monthly Archives: May 2026

Kugona

Tulo ndi chimodzi mwa zinthu zofunikira kwambiri kwa munthu aliyense, monga mmene kudya ndi kumwa zilili zofunikira kwambiri. Allah Talaa akutchula za ubwino waukulu wa tulo mu Qur’aan Majiid ponena kuti: Ndipo tidakupangirani tulo kukhala mpumulo. M’ndime ina Allah Talaa akuti: Iye ndi Yemwe adakupangirani usiku kukhala chovala (chokuphimbani ndi …

Read More »

Hazrat Abdullah bin Mas’uud (radhiyallahu ‘anhu) ndi Izindikiri wake a Quraan Majiid

Shaqiiq bin Salamah (rahimahullah), ophunzira wa Abdullah bin Mas’uud (radhiyallahu ‘anhu), akunena kuti nthawi ina yake, Abdullah bin Mas’uud (radhiyallahu ‘anhu) adapereka khutbah. Mu khutbahmo adati, “Ndikulumbira qasam mwa Allah! Ndinaphinzira ma surah oposa makumi asanu ndi awiri a Quraan Kariim mwachindunji kuchokera kwa Rasulullah (sallallahu alaihi wasallam). Ndikulumbira m’dzina …

Read More »