Ulendo wina, nthawi ya khilaafat yake, Sayyiduna Uthmaan (radhwiyallhu ‘anhu) anabwera kudzacheza ndi Olemekezeka Abdullah bin Mas’ood (radhiyallahu ‘anhu). Apa ndikuti Abdullah bin Masood (radhwiyallahu ‘anhu) akudwala matenda ake omaliza. Sayyiduna Uthman (radhwiyallahu ‘anhu) anamufunsa kuti, “Ndi vuto lanji lomwe likukusautsa?” Abdullah bin Mas’ood (radhiyallahu ‘anhu) anayankha kuti, “Chomwe chikundisautsa …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu