Daily Archives: April 28, 2026

Nkhani Yokhudza Kulowa Chisilamu Kwa Sayyiduna Wahshi Radhwiyallahu Anhu

Pankhondo ya Uhud, chimodzi mwa zowawa zowawitsa zomwe zidamuchitikira Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) kudali kuphedwa kwa amalume ake okondedwa Sayyiduna Hamzah (radhwiyallahu anhu) Amene adamupha Hamzah sanali wina koma Wahshi bun Harb Nthawi imeneyo ndikuti asadakhale nsilamu, koma Allah Talaa pambuyo pake adamdalitsa ndi Imaan ndi ulemelero okhala Sahaabi. Nkhani …

Read More »