Shaqiiq bin Salamah (rahimahullah), ophunzira wa Abdullah bin Mas’uud (radhiyallahu ‘anhu), akunena kuti nthawi ina yake, Abdullah bin Mas’uud (radhiyallahu ‘anhu) adapereka khutbah. Mu khutbahmo adati, “Ndikulumbira qasam mwa Allah! Ndinaphinzira ma surah oposa makumi asanu ndi awiri a Quraan Kariim mwachindunji kuchokera kwa Rasulullah (sallallahu alaihi wasallam). Ndikulumbira m’dzina …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu