1. Mukamaliza Swala ya Esha, musakhale kumacheza nkhani zopanda pake mmalo mwake yesetsani kugona mwachangu kuti mudzukire Tahajjud komanso Swala ya Fajr mnthawi yake. Komabe, ngati pali chifukwa chomveka, monga kukambirana ndikuchita za Dini mutha, kukambirana za malamulo a Dini mashwarah ofunikira, ndi zina zotero. ndiye kuti mudzaloredwa kuchita nawo …
Read More »Daily Archives: May 20, 2026
Osataya Chiyembekezo Mu Kusinthika Kwa Munthu Aliyense
Abdullah bin Maslamah Q’anabi (rahimahullah) anali m’gulu la ma Muhadditheen otsogola mu nthawi yake. Iye anali mtsogoleri wa ma Muhadditheen ambiri otchuka, ngati Imaam Bukhaari, Imaam Muslim ndi Imaam Abu Dawood (rahimahullah) Zikunenedwa kuti pachiyambi cha moyo wake, ankacheza ndi anthu oipa ndipo ankamwa mowa. Komabe, atakumana ndi Muhaddith …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu