Daily Archives: May 11, 2026

Kusamalitsa kwakukulu Kwa Sayyiduna Abdullah bin Mas’ood (radhiyallahu ‘anhu) Potulutsa mahadith a Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam)

Ole.wkezeka ‘Amr bin Maimoon (rahimahullah) adafotokoza za kusamalitsa kwakukulu kwa Abdullah bin Mas’ood (radhiyallahu ‘anhu) pamene ankatulutsa mahaadith kuchokera kwa Rasulullah (ssallallahu alaihi wasallam). Adanena kuti, “Nthawi ina, Abdullah bin Mas’ood (radhiyallahu ‘anhu) atayamba kunena Hadith yochokera kwa Rasulullah (sallallahu alaihi wasallam), adagwidwa ndi mantha ndi nkhawa kotero kuti madontho …

Read More »