Daily Archives: August 12, 2026

Zinthu Zomwe Zimachititsa Kuti Mdalitso Wa Allah Uchoke

Kuipa Kojambula Zithunzi Tiku lina Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) kulibe ali koyenda, Bibi Aaishah adapachika katani yokhala ndi zithunzi za zinthu zamoyo pakhomo. Nthawiyo Sayyidah Aaishah (radhwiyallahu anha) sankadziwa kuti zithunzi za zinthu zamoyo zinali zoletsedwa. Rasulullah (swallallahu alaihi wasallam) atafika kunyumba kwake ndipo maso ake anagwera pa katanilo anakwiya …

Read More »