Abaan bin Uthmaan (rahimahullah) akufotokoza kuti: Tsiku lina, munthu wina anakonza zoti amuzunze Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) ndikumuchititsa manyazi. Anapita kwa atsogoleri onse achi Quraish nawauza kuti Ibnu Abbaas (radhwiyallahu ‘anhuma) akuwaitanira chakudya m’mawa otsatira. Munthuyo anapita malo osiyanasiyana ndipo anapitiriza kuitana anthu m’malo mwa Abdullah bin Abbaas (radhwiyallahu …
Read More »
Alislaam Yeretsani mtima wanu potsatira chisilamu