Daily Archives: September 24, 2026

Kudzuka

Tisanagone, taphunzitsidwa kubwereza madua a masnoon ndikumutchura Allah. Mwa ma dua a masnoon tisanagone, pali dua iyi: اللَّهُمَّ بِاسْمِكَ أَمُوْتُ وَأَحْيٰى O Allah Ta’ala ndi dzina lanu, ndikufa ndikukhala ndi moyo. Mu dua iyi, tulo lafaniziridwa ndi imfa, chifukwa chakuti munthu akagona, samakhalanso ndi mphamvu komanso kuzindikira zomwe zikuchitika. Choncho, …

Read More »